BON KALINDO LERO PA 25 AUGUST 2025|

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 12. 09. 2024

Komentáře • 70

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Před 19 dny +9

    Guys Let's admit that politics has become a global epidemic

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah Před 18 dny

    Adzangosowa boni kalindo

  • @FiskaniLungu
    @FiskaniLungu Před 18 dny

    Ogulidwa ndi usii yekha Kalindo osadanda tikoza zinthu soon

  • @MafavukeJere
    @MafavukeJere Před 18 dny

    More fire ❤❤❤❤ the dc

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Před 18 dny +1

    Apapa UTM ikhale smart. Afufuze kuti amene akupanga ma meeting mwa chinsinsiwo ndi ndani, akapezeka , akhale chete , atolelane enawo ndikupatsana maudindo ofunikirawo akuluakuluwo. Kenaka apangitse convention. Maudindo asankhana aja akakhale opanda opikisana nawo, Ena ang'onoang'onowo akapikisane. President, SG, etc. pasakakhale opikisana nawo that's it.

  • @IshmaelMkwanda
    @IshmaelMkwanda Před 18 dny

    Exactly 🎉❤

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Před 18 dny

    Eish koma ndaama imasintha umunthu

  • @TemwaKabisa
    @TemwaKabisa Před 18 dny

    The DC ❤❤❤❤

  • @KateMunthali
    @KateMunthali Před 19 dny +2

    Koma iweyo winiko🙌usazafe uzangosowa🎉

  • @user-mv1wg2qd6i
    @user-mv1wg2qd6i Před 18 dny

    Umakwana winiko the DC

  • @MazyYanga
    @MazyYanga Před 19 dny +3

    My president

  • @EllardNkhoma
    @EllardNkhoma Před 17 dny

    President wathu

  • @HaruunWalusa
    @HaruunWalusa Před 18 dny

    Then DC bon kalindo number one ❤❤❤❤❤

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Před 19 dny +2

    Magalimoto landirani, ndalamazo idyani. Koma osaiwalira Kuti :Ngati mupange mistake, mzimu wa SKC uzakhala pa mutu panu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 18 dny

    ndiposo wa chirima skc sangakhare kwa chikangawa wanuyo

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 18 dny

    Alick nanuso inu zidwani ndarama zo zimastanic zapezeka ndinthawi yanu sangararani ifeyo wathu ndimwe mwampha kare koma miziwe kuti wamuyaya kuribe ndiposo murungu simunthu

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Před 19 dny +1

    My president Bon KALINDO

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Před 19 dny +1

    Skaliot bola ayambise chipani chake
    Akuononga UTM

  • @FarooMacolicious
    @FarooMacolicious Před 19 dny

    My President inuyo mukanakhala ndchipani chanu vote yanga mukanatengelatu🔥🔥

  • @lizzymotika3895
    @lizzymotika3895 Před 18 dny

    A vice akubwerewsa nsokonezo ndipo ndi satana

  • @AnnoyedEagleRay-lm9ex
    @AnnoyedEagleRay-lm9ex Před 17 dny

    koma inu zoona uyu amangonyoza

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 18 dny

    utm siyinathe utm yathu tiripo azarowese anthu kukarowa u present ifeyo tiri kutiko asiyeni azirubwa rubwa amenewo azigurika ndindarama zaboma zabowoka asiye adyeko nawo

  • @DrianoYakobe
    @DrianoYakobe Před 18 dny

    My president well coming

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 19 dny

    The Dc Bon kalindo number one ❤

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Před 18 dny

    Bwanji a Kalindo siimunakuwekuwe ataitana ku DPP chifukwa amapita kuchipani chanu eti?

  • @VincentMasauko
    @VincentMasauko Před 19 dny +1

    Umakwana president wathu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 18 dny

    akumadarira zimenezo za ufitizo koma akunama atengerapo kuti amasuka poti tinauza kuti sitizarowereraso zandare ndiye ndarezo azankhumudwa azawona taturukira kumaso maaaa ngati chikangawa asiye azakhumudwa amenewo autm ya sikono manganya Mr madrama

  • @user-mm3wq8qp2q
    @user-mm3wq8qp2q Před 18 dny

    please UTM fix this quick izi ai sizoona 😢😢

  • @SineeSha-bg9uj
    @SineeSha-bg9uj Před 18 dny

    Ndale ndizopanga anthu oyipa mitima we all know that

  • @EneyaKakhobwe-tq3uy
    @EneyaKakhobwe-tq3uy Před 18 dny

    Ng'alulayizeshoni booooooni kalindoooooo the DC

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 Před 19 dny +3

    When God says no, nobody can say yes.

  • @user-zg9se4rw6v
    @user-zg9se4rw6v Před 18 dny

    Kalindo leka kubendezga vinjelu vya wanthu, kuti walondolenge wutimbanizgi wako, palije icho wungabavwira wanthu, ukusambizga wanthu vakutuka mavwalo ghawanyawo, nkhuzenga nthena nadi iwe kalindo? Vilekeke lethu

    • @Creslevison-vj2sl
      @Creslevison-vj2sl Před 18 dny

      Kagwere iwe ukununkha iweyo ndani kut Uzit vilekeke ? Kavuwevuwe iwe iya ,this this democratic nation ndye usatinyasapo apa iyaaaa

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc Před 19 dny

    Our president forever DC 🔥🔥💪💪

  • @EstherChinkhata-hn8mf
    @EstherChinkhata-hn8mf Před 18 dny

    Boooom!!!!!!!!!!!!!

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před 18 dny

    Bon karido ❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @ChanceJasten
    @ChanceJasten Před 19 dny

    The DC Boooon Kalindo iweyo umatha unabwela kuzakhala

  • @user-po9yj6io3c
    @user-po9yj6io3c Před 18 dny

    The DC mwana oopsa kwambiri.

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 18 dny

    tinanena kare kuti tidutsa mzambiri ndizimenezo kopanda mayesero zinayamba murungu

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh Před 19 dny +1

    The Dccccc❤

  • @MulichaniMissi
    @MulichaniMissi Před 19 dny

    Ng'alulasation yomweyo baba Munabwera inuyo inuyo ndnyooo sss atatu

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Před 18 dny

    Ndiye kuti amatchalichi azitengera kuti mtsogoreri azimutsatira chifukwa ndi watchurch chanu? Ama church osamvera anthu oduka mituwa ayi.

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 19 dny

    😂😂😂😂😂 palibe safuna ndalama amenewo asiyeni ndi nthawi yawo nawo adyeko

  • @AlickjoiceMatchipisa
    @AlickjoiceMatchipisa Před 19 dny

    Winiko iweyo ndi kawawa ase chilima anasokoneza malawi koma anazindikila kulakwakwake ndipo anagwesa khope ngati Simon ndipo anapepesa mpake amafuna kuthetsa chipan chake

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před 18 dny

    The DC president wathu wathu wa amphawi

  • @imraanJafal
    @imraanJafal Před 19 dny

    Aaaaa Quran asaiputepo angofa okha asayambe kusewera ndi Allah

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Před 19 dny +1

    Zomvesa chisoni ndithu

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Před 19 dny

    Bwana

  • @CharlesNachidwe-et2ms
    @CharlesNachidwe-et2ms Před 18 dny

    Wa utm weni weni sangakhale mbali ya chikangawa dikilani muone

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Před 19 dny

    UTM inayo yikuwoneka kuti ndiya afiti akuyenda mumisikamu

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 18 dny

    Akatundu the DC

  • @Robertmkango
    @Robertmkango Před 18 dny

    The DC bon kakalindo

  • @ArnoldJames-e2l
    @ArnoldJames-e2l Před 18 dny

    Km inuyo bwana nd khan zina

  • @PeterChikoja-y5x
    @PeterChikoja-y5x Před 19 dny

    Kazitape

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 19 dny

    Utm idatha kale

  • @ZephinutMtande
    @ZephinutMtande Před 19 dny

    Iweyo umakwana

  • @isaacybanda-s6e
    @isaacybanda-s6e Před 19 dny

    Tiuzen bas chilungamocho

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g Před 19 dny

    Mcp yakupa kamala chilima

  • @LatifBeni-e6z
    @LatifBeni-e6z Před 19 dny

    ❤❤❤❤❤❤

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Před 18 dny

    More fire Booooon kalindoooo ❤❤❤❤❤❤

  • @CharlesMateya
    @CharlesMateya Před 19 dny

    Mbandende

  • @happychavula4469
    @happychavula4469 Před 18 dny

    Kung'alula mmmmmmm kkkkkk moto buuuu

  • @user-zo4ql3vn4f
    @user-zo4ql3vn4f Před 19 dny

    The DC🎉

  • @user-oq6ph1qq5d
    @user-oq6ph1qq5d Před 19 dny

    😂😂😂

  • @RashidJohnphirigombwa
    @RashidJohnphirigombwa Před 19 dny

    The DC

  • @BrightSauka
    @BrightSauka Před 19 dny

    zokhuza

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Před 18 dny

    Ngati unadyera ama business kuti azizemba misonkho azisanza ndalama zimenezo. Anakuuza kale a Kapoloma pompaja kuti stamp simsonkho

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda Před 18 dny

    🔥🔥🔥

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Před 18 dny

    Eish koma ndaama imasintha umunthu