BON KALINDO LERO PA 30 AUGUST WAIPHEDULASO INA UKU NDIPO WATI AMAFUNA ATAMVA KUTI WAMWALIRA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 09. 2024

Komentáře • 102

  • @WakisaNjeghenje-i2n
    @WakisaNjeghenje-i2n Před 14 dny +5

    Boooooooon kalindo mmatiyimilira akumizife ❤❤❤❤❤

  • @frankdonovanntambira
    @frankdonovanntambira Před 13 dny

    Boooooooooooooooooon Kalindoooooooooooooooooooooo chimwana Choopsa Kwambiri the DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani Před 14 dny +1

    A police a limbe kuyambilakale amatizunza zikomo kalindo powadzudzula ndikukumbuka wankulu wa police kamwendo anandimangapo mu shop opanda chifukwa zimandiwawa mpaka lero

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 14 dny +2

    Bon kalindo is a person who sended by God, and is the same God who gonna be protect the DCccccc forever ❤

  • @LenardKachingwe-p2j
    @LenardKachingwe-p2j Před 14 dny +1

    Ulemu wanu Mr Bon❤❤❤❤❤❤ more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa Před 15 dny +2

    ❤DC your the best boss
    Kukunvelani from cape Town pa boma 🎉🎉

  • @KamwanaChifundo
    @KamwanaChifundo Před 15 dny +8

    Don't give up Mr born 🙏🙏
    Ena Aja apasidwa Chibazi sakupezeka Koma iwe ndiiwe munthu woimadi pachirungamo My Allah protect u 🙏

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Před 15 dny +7

    The DC ulemu wanu boss osatopa ayi 💪💪💪

  • @JamesKachikuni
    @JamesKachikuni Před 14 dny

    Akufuna kuyambitsa nkhondo

  • @DianaMmagisa
    @DianaMmagisa Před 13 dny

    Umatha the DC awawa ndimakape nthawi Yao yatha

  • @MemoryGiftKumfela
    @MemoryGiftKumfela Před 13 dny

    The DC inuyo mulungu azikupatsan moyo wautali ndiwe hope yathu yokhayo tatsala nayo ife amalawi iwe umatiyimilila

  • @MafavukeJere
    @MafavukeJere Před 15 dny +1

    The DC ❤❤❤ my president

  • @user-zq3uf5bc8v
    @user-zq3uf5bc8v Před 13 dny

    Bonikalindo mwana oops kwambiri tiye nazo ang,alure

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Před 13 dny

    Ine ndiye mmodzi mwa anthu okupemphelerayo iweyo Booóooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooóooooooooooooooooooooooooooooóooooooooooooóooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooóooooooooooooooooooon kalindooooooooo the DCcccccc

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni Před 15 dny

    We lift yu higher man from Zimbabwe Bulawayo

  • @rabeccahmakhambera
    @rabeccahmakhambera Před 14 dny

    Booooooooooon kaliiiiiiiiiiiiiindooooooooooo😂
    Dc

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 15 dny +1

    Apolice Akumavala Zong'ambika Pathako ngati style kuli kusowa kwa uniform, Nyau ndi Apolice Panopa Sizikuyana onse muzigamba, Nthawi Ya APM Umatha Kuloza Kuti Iyo Nyau Uyo Wapolice.

  • @user-hq3lr5xm1m
    @user-hq3lr5xm1m Před 13 dny

    ❤❤❤❤❤❤

  • @Leahnyatakimkandawire
    @Leahnyatakimkandawire Před 15 dny +2

    Dolo katatu

  • @GreyThomas-chink
    @GreyThomas-chink Před 14 dny

    Keep fighting for poor people Mr Bon kalindo we proud of you May God protect you

  • @IshmaelJailosi
    @IshmaelJailosi Před 14 dny

    Abwana athu

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 14 dny

    Mulungu wathu ndi okhulupilika sadzatichititsa manyazi onse amene anapha anthu 9 aja adzadziwika sikale ayi

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles Před 15 dny +1

    The DC, wina amafuna azikuophweza ati upase 3 mita nonsense basi, osaopa the DC

  • @Jessiechirwa-n5q
    @Jessiechirwa-n5q Před 14 dny

    ❤ mulungu azikudalisa thawi zonse

  • @RichardSingini
    @RichardSingini Před 14 dny

    Koma bon umatha

  • @MadukalotOmar
    @MadukalotOmar Před 14 dny

    De do B kalindo inuyo nd bg

  • @FatimaLesson
    @FatimaLesson Před 15 dny

    Boooooooooon kalindoooooooooo😂😂 kuswa

  • @LytonSk
    @LytonSk Před 14 dny

    Kkkkkk km iweyo azukulu anga ndichani ndipanga ngoxi 😂😂😂

  • @SungeniLompwa
    @SungeniLompwa Před 14 dny

    DC

  • @SamuelKamwana-r4w
    @SamuelKamwana-r4w Před 14 dny

    DC auzeni amenewa

  • @GeraldMphande-g7e
    @GeraldMphande-g7e Před 15 dny

    My president

  • @JamesKachikuni
    @JamesKachikuni Před 14 dny

    Zaziii

  • @user-io6ql2vr3v
    @user-io6ql2vr3v Před 14 dny +1

    Ine wa police kuno ku ntaja police mr DC ndpo mukuyakhulazo ndzoona ndkuthokozeni kwambiri ndthu.

  • @AntonMartial
    @AntonMartial Před 14 dny

    Our beloved

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness Před 14 dny

    Kungoti ena tinasiya kukupasani koment yabwino kuyambira pamene tizaniza kuti mukusapota dpp ndicho chifukwa chake or boma likupanga zabwino kwayinu ndizoyipa koma mukundivesa cgisoni nkhani zanu mumayka moyo pachiswe anthu akumizi chifukwa chama boza anu koma mumene waluntawuni wamawona zinthu pamene zililiri

  • @user-kp9my5bp6g
    @user-kp9my5bp6g Před 15 dny

    Way to go

  • @PhilipChodwe-n1d
    @PhilipChodwe-n1d Před 15 dny

    Komaso 040 the DC ikungwila tchito kuipa. Bwana zoona drive wa Mira 6opn 7:00am aitenga kuti coz of Muthu modzi tikuvutika panseu Malawi wathu tikusowa kothawila kuti timpeze ndalam

  • @ChimwemwePetro-yj4gl
    @ChimwemwePetro-yj4gl Před 14 dny

    Ng'aluralisation😂

  • @MadalitsoChilinjala-f9v

    Koma saname bon ndiwe katundu boma likusowa nawe mtendere

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 Před 14 dny

    Ma Thugs Akuba/Kulanda athu-ovutika LILONGWE Self made Vendor Abuserz

  • @flimited-rw5uw
    @flimited-rw5uw Před 15 dny

    salute mr B kalondo

  • @liwemlockey
    @liwemlockey Před 14 dny

    Ndipo atikwana ndetawatopera muwavera

  • @ChimmzyMbunju
    @ChimmzyMbunju Před 14 dny

    Boos ifenso pa kwidzi amakoda kutilanda

  • @savinapili7185
    @savinapili7185 Před 15 dny

    mau amenewo a kalindo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 15 dny

    Malawi boma tilibe chitsadzo president kuyankhula dzina nduna kuyankhula pankhani ya ndege uchisilu wa MCP umenewo

  • @paulKennedy-n4b
    @paulKennedy-n4b Před 14 dny

    Bwana waoyo dzina lake ndi nchingula

  • @FredPondamwala
    @FredPondamwala Před 14 dny

    Ati zisankho mukufuna kuberazi 🤣🤣

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala Před 14 dny

    The DC

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy Před 15 dny

    😂😂😂😂😂❤❤❤❤ Kuti zinveke bwa❤❤❤❤

  • @violetpotani
    @violetpotani Před 15 dny

    😅😅😅Nde mwati white 😅😅😅ayi fenkis.. Tikuvutikira limodzi

  • @DadiraiMundandishe
    @DadiraiMundandishe Před 14 dny

    2 am or 11 AM yet president akudutsa mawa 😂😂😂😂😂😂

  • @Lucy-k6h4j
    @Lucy-k6h4j Před 15 dny

    Uyu ndiye amatiimilira

  • @ChimmzyMbunju
    @ChimmzyMbunju Před 14 dny

    Boos alakhuleni avense

  • @macksonmkandawire5718
    @macksonmkandawire5718 Před 15 dny

    Winiko Ali ndi ukali atamuna u minister mbuli iyi

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi Před 15 dny

    Kulibe apolice kumalawiko ine ndikosaso kuwapa akupanga za chibwana ndi ine

  • @IshmaelMkwanda
    @IshmaelMkwanda Před 14 dny

    Ulemu bon

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 Před 15 dny

    Mwalilani ngati mwakonda mani 😂😂😂 muwwtengeko a ndale popita kumandako akakupulumutseni ku moto ndi nsanje muli nayoyo 😅😅😅satana akakulandilani man pamodzi ndi APM wanuyo

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani Před 15 dny

    Ma delegates kudya 500000pin, wapolice 5000😂😂😂😂😂😂zodabwitsa kwabasi

  • @MauriceLungu
    @MauriceLungu Před 15 dny

    Sunama karindo aporisi arinchibwana

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds Před 15 dny

    The Dc

  • @DesmondTaulaye
    @DesmondTaulaye Před 15 dny

    A police ndi ovutikadi kwambiri jombo idatha kalekale

  • @ChristopherChimbalanga-ez5he

    Ulem wanu boss

  • @MpanjeHardware
    @MpanjeHardware Před 14 dny

    Umakwana

  • @IcraIssa
    @IcraIssa Před 15 dny +1

    Ali ndi nambala ya bon kalindo anditumizile

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 Před 15 dny

      Ineso ndikuyifuna number ya satana ameneyu

    • @auspiciousmaloya
      @auspiciousmaloya Před 15 dny

      ​@@alexandermeke6994koma ndee kapeyu mumamusatatu eeeh 😅

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 Před 15 dny

      @@auspiciousmaloya kape wa ambuli uyu

    • @tingamasi106
      @tingamasi106 Před 14 dny

      ​@@alexandermeke6994basi inu busy kumamvera za kape? Osamvera za madolo bwa? Ndekuti makape mwakumanapo

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 15 dny

    11.00am chikangawa akudusa mawa 2.30pm 😂😂😂😂😂😂 mavuto alipod

  • @Michaelmtanga-v8g
    @Michaelmtanga-v8g Před 10 dny

    ,😂😂😂😂😂😂

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v Před 15 dny

    Mau amenewa bwanji

  • @YusufuAlie-b1l
    @YusufuAlie-b1l Před 15 dny

    Police ndii agalu 😂😂😂

  • @user-mt1su7li6z
    @user-mt1su7li6z Před 15 dny

    Mbambande

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z Před 15 dny

    The D C

  • @MafunoBanda
    @MafunoBanda Před 14 dny

    Apolice akutumani lero. Ife tikufuna za report yandege

  • @WitnessKamoto-bf4pu
    @WitnessKamoto-bf4pu Před 15 dny

    Uyu amalimba mtima amwene

  • @stanleymandala8438
    @stanleymandala8438 Před 15 dny

    team mbambande

  • @MphatsoJameschipali
    @MphatsoJameschipali Před 15 dny

    Ulemu wanu

  • @NtopeLucias
    @NtopeLucias Před 15 dny

    Uyu ndi mamuna

  • @PhilipChodwe-n1d
    @PhilipChodwe-n1d Před 15 dny

    Komaso 040bwana silibwink

    • @MavutoChekeni
      @MavutoChekeni Před 15 dny

      Iwe bon kalindo Boma lapidary lidalamulapo kale koma mavuto sadathe acity ukunenawo nthawi yapitara ankathamangitsaso magenta ndiye usatinyase kuchikamwakwako

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 Před 15 dny

    Mmm muli dyooo kunvera mbuliyi?? Ngakhale zitakhala kut zinthu siziki bwino, ndie zoyankhula zake zakapeyu nkumanzinvera?? Angopereka 300.000,000-yo kwa wankulu wa mera uja Basi chifukwa chomunamizira nkhani zamabodza zakezi,

  • @DesmondTaulaye
    @DesmondTaulaye Před 15 dny

    Nkhani yo ndi yoona apolisi amangopanga zithu mwa umburi

  • @KelvinkaffaTchilia
    @KelvinkaffaTchilia Před 13 dny

    ❤❤❤❤

  • @PhilipChodwe-n1d
    @PhilipChodwe-n1d Před 15 dny

    Komaso 040 the DC ikungwila tchito kuipa. Bwana zoona drive wa Mira 6opn 7:00am aitenga kuti coz of Muthu modzi tikuvutika panseu Malawi wathu tikusowa kothawila kuti timpeze ndalam

  • @InnocentBanda-g6i
    @InnocentBanda-g6i Před 14 dny

  • @Matolataibu
    @Matolataibu Před 15 dny

    Ulemu wanu

  • @user-ts2bb2no2u
    @user-ts2bb2no2u Před 13 dny

    ❤❤❤❤❤