OPPOSITION YABWELERA MWAKALE NDIPO AKUBOMA KULIBE KUPUMA AWAPANIKIZA KWAMBIRI |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 09. 2024

Komentáře • 47

  • @EliyasKanfana
    @EliyasKanfana Před 15 dny +4

    Ngati mukufuna kupezelapo mwayi obelapo ndalama munya muona chaka chake ndichino

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 15 dny +4

    We fully support opposition leader , as Malawians we need opposition party like this

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo Před 15 dny +5

    Opposition yomwe tinali kuyembekezera ndi yomweyi.
    Osati muja anali kupangila Nankhumwa.
    Kuti chilichonse zikomo bwana.

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před 15 dny +1

    Team chaponda yabwera kuzakhala 🔥🔥🔥🔥

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před 14 dny

    ❤❤ let's support this man agalu a mcp zomwe akupangazi mutu yawo simagwila

  • @MaliroEliasi
    @MaliroEliasi Před 14 dny +1

    Asaa!!!! ndmkaesa mmat mafuta ayamba kuchipa pot mafuta ayamba kubwela pa njanji nanga lero mchaaa? Mukufuna muzngotzumza etiii?

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 15 dny +2

    Namkhumwa anadya ndalama za MCPigs.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před 14 dny

    Opposition yabwela mwa nyooo,osati leader kuchokera ku mbali yaboma yomweyo amatero

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 Před 15 dny +2

    Chaponda muwafinye a chikangawa anthu osamva

  • @ROSEKATHYOLA
    @ROSEKATHYOLA Před 15 dny +2

    Kodi ndichifukwa chani president you sakufuna kumva zonena anthu?

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i Před 15 dny +1

    This is opposition we was waiting in Malawi don't take us for the pus

  • @GeraldGomati
    @GeraldGomati Před 15 dny

    Kondwani Nankhumwa anatichedwesa kwambiri

  • @HarloMalimda
    @HarloMalimda Před 15 dny +1

    Mr Kalindo atiuza kale zokhuza kukwela kwa mafuta

  • @BartonKalumba-xf3os
    @BartonKalumba-xf3os Před 10 dny

    Simukudziwa chomwe mukunena sikuononga dziko lachakwala Malawi alipo mmodzi ma jealous yanuyo

  • @tasmania527
    @tasmania527 Před 15 dny

    Opposition ya Maizegate? maye ine.

  • @MasterMwandira-d3k
    @MasterMwandira-d3k Před 15 dny

    Chifukwa chiyani ma bridge akumangidwa ndi ndalama zochoka ku MERA? Chifukwa palibemunthu akumwesa galimoto kobanda kulipila?

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Před 14 dny

    Zauchisiru Chikangawa machende Ako

  • @sheikhjaffarwhyte2688
    @sheikhjaffarwhyte2688 Před 15 dny

    Opposition ndiyomweyi

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Před 15 dny +2

    This is wat we call it opposition not ya Nankhumwa chitsiru cha munthu kumangopanga makani koma mutu mulibemo kanthu fooolish!!!!!

  • @mkhokholasamuzonda5094

    chilegi mboleyamako

  • @MoosahChikwakwa
    @MoosahChikwakwa Před 15 dny

    Opposition must be in this way that is what we call opposition 😂😂😂😂 president himself said report is out and Moses mikuyu said opposite way who is he 😂😂😂😂😂😂 mikuyu you already in mikuyu prison to save hard labour in it😂😂😂😂😂😂unva kuocha aise😂😂😂 koma ku china upita bola osakasekula mmimba😂😂😂😂

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o Před 15 dny

    Apapa ineso ndikudabwa kuti chachitika ndichani kuti lero a mera apitise nkhani yokweza mtengo wa mafuta ku parliament? Apapa zikuchita kuoneselatu kuti kukwezaku ndikosavomelezeka. Izi ndizongofuna kubera aMalawi

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i Před 15 dny

    Adatuma dala muthu wapadera kut anene izi kod chimwendo sangakhale ochenjera kuposa tonse uyut next year tozansenxa ndi manja athu

  • @SalomeManda-c1i
    @SalomeManda-c1i Před 15 dny

    Kmat a kho nankhumwa pa nyapao amatichedwrsa

  • @user-co6sc8om5n
    @user-co6sc8om5n Před 15 dny

    Opposition moto 🔥🔥

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v Před 15 dny

    Mega farm muligawana aboma nokha nokha anthu kumizi akuvutika

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi Před 15 dny

    Achimwendo asaname kuti amacheza nawo amela ndimanyazi amenewo

  • @user-xn4if9sr3e
    @user-xn4if9sr3e Před 15 dny

    Koma a chakwera mpwitikizi amamudziwa bwinobwino? 😅😅😅

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc Před 15 dny

    Opposition amasokoneza nd nakhumwa uja

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 Před 15 dny

    chaponda sangaluze kawiri kapena kuwiro
    tiyeni naeoni amatha chipongwe pokwanilitsa ( mcp )

  • @fatimaamidu3967
    @fatimaamidu3967 Před 15 dny

    Kodi Kubomaku Kuli chimwendo Banda yekha

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v Před 15 dny

    Mafuta asakwere

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Před 15 dny

    Akuononga ndalama kwambir daily umva chikangawa wapita kwakut ndie kt

  • @LastonAdson
    @LastonAdson Před 15 dny

    Buzi izi zatikwan khani ndi mademo. Bac no. Solution apa za. Chamba ayi

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Před 15 dny

    Iweso ndi garu

  • @LydiaManzy
    @LydiaManzy Před 15 dny

    Misewu yake it amera wo mavuto wo ndi awooo

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 Před 15 dny

    iwe wa mcp pamtumbo pako ndi co.mittee yakoyo

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Před 15 dny

    Mcp kutumbwa khunguru party

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Před 15 dny +1

    Mumachedwa kut a Dpp kumeneko ndiye kubwera!!!

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Před 15 dny

    Za opposition zaboza izi

  • @ChrispineJonathan
    @ChrispineJonathan Před 15 dny

    Mutenge ndalama za tollgat

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Před 14 dny

    Zauchisiru Chikangawa machende Ako

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Před 14 dny

    Zauchisiru Chikangawa machende Ako