Mdulidwe Ndi Oyipa Koopsa - Ukunokolelani Injini

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024
  • Kanani Mdulidwe

Komentáře • 103

  • @RargieMediaclassic
    @RargieMediaclassic Před 19 dny

    Ife za mdulidwe tinatengera ataumbalidwa yesu

  • @statuspremier
    @statuspremier Před 13 dny

    Ase unfiltered, umakwana big bro

  • @user-hc9hc3dk5o
    @user-hc9hc3dk5o Před měsícem

    Ndimaona ngati ndimva mukunenapo kuti mdulidwe ndi oipa.but I quote you saying you can do it later in life.

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 Před 2 měsíci +1

    I support u bro on this topic whatever u say is truth

  • @user-qe2lz7mx7u
    @user-qe2lz7mx7u Před 3 měsíci +2

    Iwe mdulidwe unayamba ndimakolo athu ndipo ngakhale Abraham anadulidwa end zimene ukunenazi ife tinapita kusukulu timaziwa zambili kupotsa iwe. Ukunena ma 20s if ndi am 80s nkhope ngati kumatako kwa nguluwe ndiwe osadula ukuzibakila wekha

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Před 3 měsíci +1

    Iwe ine ndinadulidwa 1990 kulibe ma bungwe, uli ndi bvuto aise ineyo yanga ndi machine

  • @user-xy4hq6sx7v
    @user-xy4hq6sx7v Před 3 měsíci

    Yesu abulahamu and many more anadulidwa kunalibeso HIV YO iweyo bayenda ndi gaga wakoyo ndinkakuona ngati wanzeru atumbuka ndinu vinthere basi vizereza

  • @JaruMakwinja
    @JaruMakwinja Před 3 měsíci

    Iweyo nkhani imeneyo mulinayo umboni kodithu mdulidwe ziwunabwere ndi azungu koma ndi lamuro lontchokera kwa mulungu genesis 17ves9 Abraham naye anadulidwa yesu naye anadulidwa koma inu mumvekere akuti unali mtima

    • @frankbanda113
      @frankbanda113 Před 3 měsíci

      Nde baibulo analemba ndindani? Mesa azunguwo

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 Před 2 měsíci

    Kudulisa kwa chani zopusa basi

  • @MilianoMinat-jn1bi
    @MilianoMinat-jn1bi Před 3 měsíci +1

    Ndipo iweyo mmene ukuonekeramo ukhoza kukhala ndi chigaga chambiri

  • @ImannchisomoHakhimu
    @ImannchisomoHakhimu Před 3 měsíci +1

    Man kangodulidwani kudulidwa ndinkwabwino.

  • @BannetNansongole
    @BannetNansongole Před měsícem

    Ine ndinadulisa chifukwa kusogolo kwa shafuti yanga kumathetheka kuma panga zilonda timabala anyway tinadulisa kale basi

  • @emmanuelmulli265
    @emmanuelmulli265 Před 3 měsíci +1

    1.Too late tinapita kale
    2.Zinayamba kale mmbaibulo

  • @d-foxhd8369
    @d-foxhd8369 Před 3 měsíci +3

    Awesome show, I agree with your views...I would never circumcise....I don't see any valid convincing reason for that

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Před 3 měsíci +1

    Mwayamba kunamiza anthu akulu

  • @OsmanPatrick
    @OsmanPatrick Před 3 měsíci +1

    Iwe machende ako even baibulo linanena kt mwamuna aliyese ayenera kudulidwa nde iwe ukutsutsana ndi mulungu mapwala ako iwe satana

  • @ManzyLouis
    @ManzyLouis Před 3 měsíci +1

    Izi nduzowawatu kwa munthu amene anadulidwa kale 😂😂😂😂

  • @kelvinchonjowa2985
    @kelvinchonjowa2985 Před 3 měsíci +1

    🤣🤣🤣🤣 ng'alura aise timakutsatira 🙌🙌

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 3 měsíci

    Dulidwe ngakhaleso Yesu adadulisa ndiye inu muti chani

    • @StarfordKAMOTO
      @StarfordKAMOTO Před 3 měsíci

      Kkkkkk yesu anamudula ali mwana komaso sichinali chisakho chake, chisakho chake chinali chosakwatira, chilichonse chinathera pa yesu mwina simumaziwa

  • @charlokapalamula9299
    @charlokapalamula9299 Před 3 měsíci +1

    Mukatero inuyo simunadulidwe... 😂

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias Před 3 měsíci +1

    Phwala la mtumbuka iwe mbolo yosaduluyo

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 Před 3 měsíci

    Nyimbo ilinyatwa,..menyani remix bwana wane

  • @user-pl8ll9um2p
    @user-pl8ll9um2p Před 3 měsíci

    Izizi aise ukunama ndinapangitsa 20 Years ago koma panopa sindimawona vuto

  • @Chifundo-ph1gs
    @Chifundo-ph1gs Před 3 měsíci +1

    Chilungamo chimaphweteka kulii akunena zoona

  • @Benty_Pro
    @Benty_Pro Před 3 měsíci +1

    Iyiyi Yandiwaza Heavy... koma Gulu likwiya🤣🤣🤣... Cos Honestly palibepo logic

  • @JaruMakwinja
    @JaruMakwinja Před 3 měsíci

    Kodi inuyo muli limodzi ndi Paul kukhanitsà mdulidwe zimuzalowatso mnyumba mbuli ya munthu

  • @user-xs3nj1es1r
    @user-xs3nj1es1r Před 3 měsíci +1

    Kkkkkkkkk kukubweraku anthu osadulidwa ife tikunyengerani azikazi anu gayz ine ndili pheeeee zodulisa zijah zompusa ine sindigadulise

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci +1

      umaziwa axse...osamatengeka ndi zopusa

  • @MdRahim-nw2md
    @MdRahim-nw2md Před 3 měsíci +1

    Kunyero kwako galu iwe

  • @user-rl3ku3yo6o
    @user-rl3ku3yo6o Před 3 měsíci

    kuteroko nganga Wadzadza ndizomwe ukuyakhula nazo

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Před 3 měsíci

    Mukamapanga boza lanulo tisiyano kumakusatilani cz mukuchulusano boza sopano inu mdulidwe mukanene kuti mdulidwe ndi oipa inu ndi aboza mwamva

  • @thabitiesulaiman6194
    @thabitiesulaiman6194 Před 3 měsíci

    Mdulidwe amene anayambitsa ndi mwiniwake amene analenga dziko osati azungu ayi koma mulungu yekha basi komaso azunguo amadziwa kuti mdulidwe asilamu ndimene apanga kushokela kale ngakhale American asanabwele koma kuti anene kuti chisilam ndichimene chikulondola amawona kuti chsilam chipita patsogolo kapena kutchuka m.mene chatchukilamu mdulidwe yesu anapanga Abraham anapanga mose anapanga Joseph anapanga ndeinu ndindani kuti munena kuti mdulidwe ndi oyipa mdulindwe ndiwabwino chifukwa mulungu akune mu Bible komaso quran amafotokodza ubwino wadulidwe ndichilamulo chamulungu

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      nde analengelanji kachikopa?

    • @user-pj7rl5fq6p
      @user-pj7rl5fq6p Před 3 měsíci

      Ngati mukuti bible linane za mdulidwe bwanji mutipatse verse yake tidziwe ko...
      Komaso ngati mulungu mukuti ananenapo zamdulidwe ndipatipo?
      Kodi mulungu NDI oputsa kulenga munthu osadulidwa?
      Ngatidi mdulidwe unachokera Kwa mulungu bwanji amaleka kulenga munthu odulidwa Kale...
      Kudulitsa ndi tchimo pamaso pa mulungu

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      sayankha imeneyo!

  • @williambema2305
    @williambema2305 Před 3 měsíci

    Eeeeh nde bufu cake yopanda nyemba yingaoneke bwanji 😂
    Shapeless yeniyeni😂😂

  • @AbufarihiyyaMussah
    @AbufarihiyyaMussah Před 3 měsíci

    Zikatelo yakoyo yosadula kukula konseko asiyen anthu adulitse

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ru Před 3 měsíci

    Ndikumalawikokha anthu ena mumazisankha osadula akazakowo umathila madeyawo

  • @HusseinTumamu
    @HusseinTumamu Před 3 měsíci +1

    Kuteloku mkuluyu akuyenda ndi Gaga kumbolo

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q Před 3 měsíci +1

    I agree with you bro

  • @user-ti8ds7iq8z
    @user-ti8ds7iq8z Před 3 měsíci +1

    Mbuzi iwe

  • @NelsonWaiti
    @NelsonWaiti Před 3 měsíci

    Ndiwe mbuli yophunzira.😂😂😂😂

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa Před 3 měsíci +1

    Kkkkkk komaaiseee

  • @emmanuelmakwati6915
    @emmanuelmakwati6915 Před 3 měsíci

    Anthu mumangotengeka zili zonse anakungwanjulan 😂😂😂😂

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 3 měsíci

    Mmmmmmm komanso nde zosemphanatu

  • @MisheckBanda-ho2py
    @MisheckBanda-ho2py Před 3 měsíci

    Ndoti achipatala dopusasoka 😮

  • @ThomsonNgoma
    @ThomsonNgoma Před 3 měsíci +1

    ngati munthu ukudulitsa ndi chifukwa choti osakhale ndi gaga, ndekuti munthuwe sumadziwa kusamba and naturally unve uli nawo! ukhondo ukuvuta bwanji munthu oti umalowa ku bafa every day, ndekuti simmaitsuka or what kuti mpaka kupange gaga....ukhondo should not be a reason for circumcision!

  • @denniskachande
    @denniskachande Před 3 měsíci

    Akuluwa akusowa zonena

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Před 3 měsíci

    Kupusa ndikumeneko ndiwe galu kwabasi

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 Před 3 měsíci

    Iweyo ndi katundu waboma

  • @chitchohistorical1036
    @chitchohistorical1036 Před 3 měsíci

    Ndewe galu wachabechabe 🤣🤣

  • @gidyonmshani5259
    @gidyonmshani5259 Před 3 měsíci

    Chitsilu iwe dzakutela dzoyangura

  • @STANLEYTHOM-mw2gc
    @STANLEYTHOM-mw2gc Před 3 měsíci

    Nsana okhotawo

  • @ShaliBasket
    @ShaliBasket Před 3 měsíci +1

    Satana iwe wasowa zolengeza if not sekani channel chanucho

  • @muopeni
    @muopeni Před 3 měsíci

    Akulu 🔥🔥🔥

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 Před 3 měsíci

    Bro Ife nde we already did circumcision 11years ago,..nde tipange bwanji...tikadula kamsonga kambolo yamphaka kubwezelesa

  • @user-ix7st4ec8k
    @user-ix7st4ec8k Před 3 měsíci

    Kod adawa akuti bwabji

  • @RelexRest
    @RelexRest Před 3 měsíci

    Iwe ndi wan ase part2 tpatse 😮😮😮

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos Před 3 měsíci

    Subject iyi sinsndiwaze

  • @STRATADATA-KB
    @STRATADATA-KB Před 3 měsíci

    Very true

  • @SinyoroMoyo
    @SinyoroMoyo Před 3 měsíci +2

    Kodi satana oyankhulira palirimeyu akuti chani,mtumbuka opanda mzeru kumayankhula chikunja pamenepo.mano odzadza mkamwawo galu iwe .topic iyi yandinyasa mtumbuka osadulidwa busykumaonera ma blue movie satana wa litata wandinyasa and i was not expecting this shit from you .taphumzira kuuza anthu zinthu zoti tipindulira osati zimenezi fuck offf

    • @frankbanda113
      @frankbanda113 Před 3 měsíci +1

      Kukufunsani inu kut why munadulisa simpita deep chifukwa chake. Mziti chipembezo kapenaso simfuna kutenga HIV , nde umbuliwo kupanga zokakamizidwa, not kut panokha mfikepo. Enanu ndinu odulisa kamba ka fanta 😂

    • @SinyoroMoyo
      @SinyoroMoyo Před 2 měsíci

      Sorry am not a man

  • @DaudRashid-sp3sk
    @DaudRashid-sp3sk Před 3 měsíci

    Chimutu chopindikacho galu iwe

  • @EmmanuelMponda-ig9bm
    @EmmanuelMponda-ig9bm Před 3 měsíci

    And Ambiri sakuberekamnso 😭

  • @user-ir8dd8lm1c
    @user-ir8dd8lm1c Před 3 měsíci

    Bodza Leni Leni ili ife timadya 4 rounds daily size kukula yanuyoso kuchepa🤣🤣🤣🤣

  • @JefinalaChimthunzi
    @JefinalaChimthunzi Před 24 dny

    😂😂

  • @YughozMaonga-ft2ny
    @YughozMaonga-ft2ny Před 3 měsíci

    Our generation, ladies hate mamuna owazila changu 😂😂😂uthetsa chabe zibwezi kunjaku 😂😂

  • @samueMicheal
    @samueMicheal Před 3 měsíci

    Ambili odulidwa amwalila ndi HIV enanso akudwala mpaka Pano . asatipusitse amenewa mbale Wanga. email mwa iwo tikuwawona athelatu

  • @LouisAndrew-jr1yj
    @LouisAndrew-jr1yj Před 3 měsíci

    Inu2 musocheretsa anthu🙄🙄🤔

  • @hastingskondwani1066
    @hastingskondwani1066 Před 3 měsíci

    I didn't know you are a hip hop head

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      Of course !

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      Koma of course ndife ma rootsman.

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga Před 3 měsíci

    😂😂😂😂😂....umatha aise.pala tikatinge muwelenge biology..ise mbwe nkhuma videoo...😂😂😂😂😂

  • @user-pw4dv1el3d
    @user-pw4dv1el3d Před 3 měsíci +1

    Is not like that. Circumcision is from Bible. Not the thought of any one's 😅

  • @thomgwayi8138
    @thomgwayi8138 Před 3 měsíci

    Hahah kkk

  • @JhpiegoMalawi-yj8bm
    @JhpiegoMalawi-yj8bm Před 3 měsíci

    Aaaaa iwe mdulidwe si okakamiza akulu is voluntarily ife timawadula munthu akadulidwa sizoti matenda ayi imakuteteza ku ,matenda auzeni anthu chilungamo sukudziwa kanthu make your another proper research ife kumva kukoma ndi mindset yako

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      in case you dont know ana akudulidwa all over the world.

  • @Sharif_Ys_Salim
    @Sharif_Ys_Salim Před 3 měsíci

    Kodi iwe mzeru ulibiletu eti? 😂😂😂
    Ndi anthu ohohowana yemwe angasapotepo izi...
    Iwe Mulungu ndi iwe zindikira ndani?
    Kodi amkawawuza Abraham kuti adudwe aja mukuwaphweketsa?
    Mwene Kwatirani, khalani ndi mkazi wanu, you know need plastic over intercourse.
    I have to get circumcised.
    Indeed circumcision is prevention for STIs...
    Iwowo angozindikira mochedwa kuti kudulidwa kumateteza kumatenda opatsilana pobhozana, koma atumiki anawuzidwa kale kale, inuyo mwangokhala kuti ndinu anthu makani basi....
    Zambiri mbiri zoti zinanenedwa ndi azitumiki amulungu koma mumakhala kuti simuzivomereza, mpaka mukuti a science atapangapo kafukufuku....

  • @JamusMigo-tk4mk
    @JamusMigo-tk4mk Před 3 měsíci

    I'm out with u nsosense

  • @ebrahimjannaphiri4715
    @ebrahimjannaphiri4715 Před 3 měsíci

    He talks bull shit

  • @Aladeen_265
    @Aladeen_265 Před 3 měsíci

    This video is trash.. sumaxiwa kanthu za VMMC

    • @mutafire
      @mutafire  Před 3 měsíci

      Tiuzeni

    • @Aladeen_265
      @Aladeen_265 Před 3 měsíci

      @@mutafire tomorrow, this is 12 :30 midnight, Malawi local time

  • @JaruMakwinja
    @JaruMakwinja Před 3 měsíci

    Kodi inuyo muli limodzi ndi Paul kukhanitsà mdulidwe zimuzalowatso mnyumba mbuli ya munthu