Koma Mimi inuyo aaaa, munabwera kudzatilimbikitsa ndithu🥰, malamgizo abwino achilimbikitso,like my comment I want to come again fokika mmawa tikwanitse 5 million viyuzi🔥🔥🔥🔥🔥
Hit 🔥 ingokhala national anthem ya 🇲🇼 Malawi basi🙌🙌🙌.. Muona mmene anthu tingamalimbikilile mwatokha. Yakalei mmmhh ipume kae ili too much 😔. Miracle iyiyi olo ba neba aziimba nawo. Congratulations 🎊 🎈
Nyimbo yachilimbikitso Mamie.... Nyimbo yoti ukamaimvela yosatopetsa yokha mkumakupatsa ma plan.... Nyimbo ndaikonda iyi.... Ambuye apitilize kukupatsani nzeru zakuya ndikupitiliza kutidalitsa mnkudzela munyimbo zanu mamie.... Love you
Your musical intelligence never fails you. Great power and control are all there. Your booming voice and bags of character in your tone unceasingly amuse and bless us. May you live long Miracle
Wow this song has made me feel encouraged I will never give up I will keep on pushing until zitheke zaweni kunyozetsadi bola zako umadya mwaufulu or zili zochepa ...such a good song with a powerful message keep it up Miracle 🎉🎉🎉🎉❤
Ine zomapanga comment sikwenikweni koma trust me Miracle iyiyi wandikumbutsa those good old days ndikumvera nyimbo za amai ako,,iyi waswa ndipo unabwela iweyo
Koma Mimi inuyo aaaa, munabwera kudzatilimbikitsa ndithu🥰, malamgizo abwino achilimbikitso,like my comment I want to come again fokika mmawa tikwanitse 5 million viyuzi🔥🔥🔥🔥🔥
Can someone like my comment ndikabwelenso cos this is wow
Thanks alot
For sure bro,apapa ndiye was waiting bomba mwanayi
@MiracleChinga limbikirani sister, this is the great hit,pitilizani ndithu Peter from RSA
lero ndimati simpita Ku business but after listening to the song basitu ndanyamuka
Apapaa nde you are bringing back Grace Chinga. Nyimbo zoti you can sing along and learn something. Keep it up!!
Grace must be so proud honestly
I don’t know how to thank you enough every one watching this song daily on this channel will testify in Jesus name God bless you all lovely people❤
You are a true copy of Grace. Keep it up
This song deserve million view in a month.
Miracle beautiful encouragement
Ladies tchukumani osaziyang'anira pansi.
Thank you lovely people for the support the love I appreciate let’s keep on viewing everyday until we make it 💃🏻💃🏻💃🏻💃🏻🙏
Nice and powerful!!!!!
Iyiyi mpakana 1 million views
Wow!!! The way I love this song, continue teaching through songs .this is powerful
Am Zambian and In ❤with your songs 🎉🎉🎉🎉
Ndipo it's on my status everyday nyimbo iyiyi waiumba
Your loved by many dear keep the fire burning
Uthenga wabwino,kutchena,vedio kukongola,chivoice mbambade,production yabwino aaaa mwapha nyimbo iyi 100 pa 100
Everything on point
Ndipo 100%
Mwatilimbitsa mama tithamangadi
Proud of u dear.... ndithamange inee🙏
Miyala ija is very important,ikachuluka umamanga nayo nyumba, beautiful Miracle Chinga...
Abale pangani zoti ndibwelenso❤
Bwerani basi
Koma mulungu yemwe amakupasa nzeru zomalemba nyimbo chonchi zi mmmm timuyamike nyimbo mwabebesa iyi it's as if mwaimbila inesotu mimi🎉
Miracle chinga wow...her fans lets gather here😍😍
We are here already
Tilipo kale ❤
Nyimbo yolimbikisa iyi God continue bless you Mimi
Amen amen 🙌🙌🙌
Tilipo
This is nice, quality video,the outfits were giving,nyimbo yopatsa chilimbikitso
Miracle nice composition. Iyiyi wapha Mwana Iwe. Your mum is happy
Thank GOD watipatsa zochita,,, kusatulutsatulutsa kwako kwa nyimbo kwabala zipatsobzabwino...... Nyimbo yabwino
Nyimbo iyiyi uphula nayo aseh. NGOs will come for it. Well done mamie
Credit to the producer he understood the assignment... this is nice Miracle 🔥
My Zambian people let's gather here we have a meeting 🇿🇲
Let's gather here Zambians miracle fans.Miracle you're a vibe mami
Tilipo,,love u Mimi
Miracle nyimbo mwapha iyiii it's so encouraging we really have to be self empowered and hard working 💪
Powerful message miracle❤❤
Miracle zomwe wayambazi ndayamba kukonda nyimbo zako🔥🔥🔥 uku ndiye kubwera🔥🔥🔥🔥 poangira vn ndipati ndoyipatse moto bwino 🔥🔥🔥
Eti vn wandiwaza bwanji
Apapa Grace chinga uja alimoyo ndinthu miracle wadza sure
Ndalimbikitsika, inetu ndi nthamanga once again congratulations mami mwapha nyimboyi🎉🎉🎉🎉
Hit 🔥 ingokhala national anthem ya 🇲🇼 Malawi basi🙌🙌🙌.. Muona mmene anthu tingamalimbikilile mwatokha. Yakalei mmmhh ipume kae ili too much 😔.
Miracle iyiyi olo ba neba aziimba nawo. Congratulations 🎊 🎈
Ndangoona pa Mikozi basi tu akuthamanga mzaonere🥳🥳
Nyimbo yachilimbikitso Mamie.... Nyimbo yoti ukamaimvela yosatopetsa yokha mkumakupatsa ma plan.... Nyimbo ndaikonda iyi....
Ambuye apitilize kukupatsani nzeru zakuya ndikupitiliza kutidalitsa mnkudzela munyimbo zanu mamie.... Love you
Thanks alot for 44k views let’s hit 200 🎶🎶🎶🎶🔥we can do this people
Yes we can do ❤❤❤❤❤ in Zambia 🇿🇲 we are with you mama mitrick
Yes we can do ❤❤❤❤❤ in Zambia 🇿🇲 we are with you mama mitrick
Ndiye iyi ndi nyimbo yapatali. Akudslitseni Yehovah.
I like the vibe in you ❤ maka the confidence 😌 the music video s good as well
Don't worry mama
Wow🥰🥰this is great Miracle....Mulungu apitilize kuyikizabe nyimbo za pamwamba mwa iwe ....iyiyi wapha 💯
Iyi nde yabwera ,,inde tithamanga mimi❤🔥🔥1M today
Your musical intelligence never fails you. Great power and control are all there. Your booming voice and bags of character in your tone unceasingly amuse and bless us. May you live long Miracle
Miracle this is nice 🙌🔥
Nyimbo yokoma . I don't usually finish watching a music video koma apa eeeeeee waswa
Grace Chinga is still alive through you Mamie
This is most of the amazing songs
Thank you Chinga for the encouraging song I appreciate your work, much love from Zambia.
Ineyo ndilibe zoyankhura ndingoti miracle kukazakhara kotheka tsiku Lina uzanditenge munyimbo zako
Wow, miracle this is so on point , everything on point , God bless u
Mulungu odzwa kudalisa aonjezere luso mwaiwe❤❤❤
Mbamband❤❤❤Mulungu aonjezera nzeru zakuya nyimbo yachiphunzitso
Iyiyi mwapha amwali ndipo zonse so on point tu
This is good music @miracle!!! Well composed and the video altogether is a top-notch!!!
Nyimbo mwakazinga iyiyi mamie🥳🥳🥳🥳🥳🥳
This is beautiful, message on point... congratulations for such a beautiful music.
Iyi nde miracle wapha muli uthenga umu
Tears of joy mwandikumbutsa grace chinga
Welldone miracle chinga so God voice
Been smiling throughout the song, beautiful characters and nyimbo yolimbikitsa
Wow this song has made me feel encouraged I will never give up I will keep on pushing until zitheke zaweni kunyozetsadi bola zako umadya mwaufulu or zili zochepa ...such a good song with a powerful message keep it up Miracle 🎉🎉🎉🎉❤
Eeeesh in love with this one nsaname....kupempha kutukwanitsa😍😍😍😍😍😍
Amen, what a great message.God bless you mum💞💕💕💕💞
Miracle ayi zilibwino kwambiri. Ambuye alemekezedwe. Proud of you❤
Grace chinga alipo mwana miracle voice ngt mayake
Mulungu knew Grace was a blessing and then blessed us with Miracle 😭😭❤️❤️❤️🙏🙏
Nyimbo yabwinotu mammie yachilibikitso kwabasi ❤️❤️
Go girl go, this is very beautiful,apapa tikulimbikitsika
This is wonderful talent, God ur so great. This is What we expect from u miracle.
Wow , I feel the presence of Grace chinga. Keep up the good work miracle.
Nyimbo iyi imadalisa heavy keep it up
Ure blessed dear keep the fire burning, inu simunakhumudwiseko ndi nyimbo zanu
Moto kuti buuuuuuuu,Chinyimbo mbambandeeee🎉🎉
Ngat ndilire mwamva Inu mmmhhhh very beautiful
Izi nde nyimbo zomwe timazifuna kuti tizimvera. I hope bundle yanga yapita koyenera. Nyimbo izikupasa mphunziro komanso chilimbikitso
Nyimbo waimba iyi so encouraging to women and girls
This song should be sold even in drug stores coz eeh ... miracle mwapha iyiyi
Song ya bho heavy 🔥 the message and vocals on point ☝️🔥🔥🔥🙌🙌🙌
On behalf of all your Zambian fans we love u nd yo music 💚💃
Like the song so much, keep it up Miracle
This is a nice tune and the message is just wow as usual. Thanks for this. Recieve your flowers 🌺🌹
Iyi yokha ili bho.100%from me.keep the fire burning.the world needs pple like uu
Nyimbo yophunzitsa iyii miracle keep it up 🔥🔥🔥🔥
Out here kuipanikiza nyimboyi😊... Muli uthenga umu
Good work, thanks for bringing back legend your late mom❤️❤️❤️
Muitíssimo obrigadissimo Milagre Chinga pa music imeneyi.
Miracle iweyo umatha ndikungobwerezabwereza kumvera eshiiiiiii
Wow ine chimwemwe mu mtima sikadza kokhasooo tithamangebeee basii yesu wathu pa pambalipaaa
Nice nyimbo,zonse zili wow, keep it up🥰
Wowwow wow! Congratulations mimi keep up the good work
Dolo kwambr Chinga .... full of maturity 💪💪💪💯
Ine zomapanga comment sikwenikweni koma trust me Miracle iyiyi wandikumbutsa those good old days ndikumvera nyimbo za amai ako,,iyi waswa ndipo unabwela iweyo
Mmm this is something else wapha miracle congratulations 🎉
Wow🎉mwanyimbo zonse iyi ndi 1 ❤
Powerful song ndipo muli chi message 🔥 🙏 pangani zoti ndibweretso good people 🥳❤️💃
Wandipatsa chilimbikitso mwana iwe, 😢😢 misonzi yachimwemwe😊,
This is the best song ever. Of all the songs this is the best to me. Keep it up
U have really encouraged me🎉🎉🎉🎉🎉 miracle fans let's gather here❤❤❤
Nice one nyimbo ili bwino iyi ❤❤❤❤❤ My God continue bless your talent like mother like daughter
Ma dance mpaka mlenji
I look at this video and am very proud of what your journey has been like this far. Very proud. Nice one Miracle!
I love the way you have dressed this is the picture of our late chinga keep that up
I can't hold my tears when I see her performing like her mother, pitilizani Mai grace kuusta mwamtendele
Wow this is awesome go Mimi go hire ❤❤❤❤
I have watched it countless times.i love the video
wabwera mimi...congrats❤❤ uthenga wabwino
I love the outfits.... Well done Mimi❤
Nyimbo zako ine ndiye sizimandisangalatsa .....koma na iyiyii aaaah wabwera iweyo ...ndikumaivera tsiku lonse! 🤸💃💃keep the fire burning🔥🔥🔥
Miracle 💕 iweyoo mhuuu ine mpakana misonzi kumukumbukira Grace eeeeiish Grace sanafeyi
Lozereni poti mkomente with an audio, funa my'imbe likhweruuuuuu🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Nice piece. My favorite. Thumbs up
hello, if you are in 2094 I want to tell you that I was here before you in 2024
This is great Miracle May God continue to use you powerfully
Zimakukhalani mamie mumatipangitsa kt tikhale ma happy tikavera song zanu 🤩🥰🥰
Wooow nyimbo yabwino iyi Miracle tiyeni tizithamanga azimayi tidalire zathu zaweni zidzetsa mnyozo
Glory be to God,I really like the song.Full of touching message
Enjoying the video from Zambia ❤❤❤