Komentáře •

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w Před 4 dny +11

    Ndiwe opusa kwambili bwanji iweyo osamuimbila 4n pailot kt pachitika mishion mukafika kulilongwe musanyamuke mbuliyako galu olo unene ndiye upindula chan munthu adamwalila kl

  • @DicksonMike-q5s
    @DicksonMike-q5s Před 17 hodinami +1

    Ok ngati ndi choncho Kodi panalibe njira yoti mukapelekela chenjedzo kwa oulutsa ndegeyi kapena crew ya a VP kuti ndgeyi isauluke.kuti mupulumutse myoyo ngati zinali zovuta ok nanga bwanji osadikila abomawa atulutse kaye lipoti lawolo kenako inuyo mubweletseno umboni wanuwo.

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Před 4 dny +4

    Kukomera kwake nkhayi akuyamba ndi kuti (akuti)kusonyeza kuti ndi za mmaluwa ndi anthu aja kuphunzilapo pa social media 😅😅😅

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 4 dny +4

    I doubt if this guy really works with the airport department, listen to him properly

  • @TimothyMoyendah-ih1qq
    @TimothyMoyendah-ih1qq Před 3 dny +2

    Ulibe umunthu iwe😢why you didn't tell them kuti something is going happens ndim'mene ukunvela or ukadamuimbila pilot-yo kt please usanyamuke...😢😢😢😢

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Před 4 dny +3

    Anthu ngati awa anthu osusa boma atetezeni ndikuwapasa chitetezo chokwima kuti anthu omwe akufuna kuwapanga chipongwe asawafikile please awa ndi mawumboni amphavu ku dziko lathu la malawi

  • @felixthomas1781
    @felixthomas1781 Před 13 hodinami

    Munthu wosaphunzira ngati uyu, airport yake iti yomwe angagwire ntchito. Musazilowese chibwana zinthuzi. Abale athu aja adafa imfa yowawa kwambiri. Musamale

  • @Sascar-oj4wi
    @Sascar-oj4wi Před 3 dny +1

    As long as you are not mentioning your name man that is a lie. A person who fights for the truth never hides his or her ID... be calm ... don't tell us what you've been told to say... mugjna azanu nkhani iwavute bas..

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda Před 3 dny

    Ukhale chete Ngati umadzuwa ukananena Kuti asapite ndiye ukufuna uwoneke wabwino

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 3 dny +1

    Ndachitsilu amenewa bwanji pathawi imene chilima amakwela degeyo bwanji ndichitsilu iweyo galu wava bwanji osauza athu kuti asamwele

  • @moffatchauluma171
    @moffatchauluma171 Před 3 dny

    Kungotiwawisa mutu bas, kachindere aka mwee

  • @DoreemSemu-ho3lt
    @DoreemSemu-ho3lt Před 4 dny

    Litania lamagazi Ambuye yesu mutichitile Ife chifundo Amen

  • @SungananiMilliasi
    @SungananiMilliasi Před 20 hodinami

    Ndy olo uwulule mza ntchito chani??, bwanji sunaulule kwa anthu anthu anamwalilawo.?? Bwenzi utapulumutsa miyoyo yambiri

  • @ABDULLAHUTHMAN-vj4vs
    @ABDULLAHUTHMAN-vj4vs Před 4 dny +1

    It's late now coz mukanayenera kunena zimenezo before ndegeyo kupanga ngodzi😮

  • @giftmuluwaza7483
    @giftmuluwaza7483 Před 20 hodinami

    Ngati unawudzidwa kale kuti ndege sibwera bwanji sumanena

  • @KawonaSingini
    @KawonaSingini Před 3 dny

    Iwe ndiwe wopusa kwambiri nde ukunena pano wat is your benefit now ndiwe galu kwabc athu anamwalira kale amalawi bwanji bc kufuna ku ntchuka pa social media asaaa

  • @user-tr6uh3mc2b
    @user-tr6uh3mc2b Před 3 dny

    Kunama akungofuna kuti pusinsa ameneyo osadabwa kuti sindizinchula dzina why, nde kunamako

  • @user-pj9rs6vj8x
    @user-pj9rs6vj8x Před 3 dny

    Ndiwe chitsiru zedi chomwa madzi ometera bwanji ukaleka kuyakhula ndi anthuwo zinthu zisanachitike?ndiye ukuoperanji kuzitchula dzina ukudziwa kuti ukuyakhula bodza ndinkana ukuopa chitsiru iwe kobasi

  • @amourvido8027
    @amourvido8027 Před 3 dny

    Mbuli ngati iyi ikagwire ntchito ku airport kuti chan? Aaaah pena paketu magaye

  • @johnfred2525
    @johnfred2525 Před 2 dny

    Iweso unapha nawo ukananena b4 fuck happen tangosungani zithele kukhosi. Munthu ofunikila anafa and sangabweleleso

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 3 dny

    Athutu akudziwa kale chilungamo chake zaifa yachilima ndiye inuyo basungani umboniwo kunyumba kwanuko eetu

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh Před 2 dny

    Uyu waboza nanga bwani sunalengezese pa sochomibiya zaboza izi

  • @AliceMbewe-yi1pw
    @AliceMbewe-yi1pw Před 4 dny

    Too late to save jerusalem 😢

  • @AbubakarKalembo
    @AbubakarKalembo Před 3 dny

    Ulibe nfundo nde wapindulanji poti zinachitika kale unali duu nsunu wako

  • @AufiThera
    @AufiThera Před 3 dny

    Mukudikila Chan abale tiuzilenintuni asanapheni aziwa kuphawa

  • @SamuelJohn-pc3ls
    @SamuelJohn-pc3ls Před 4 dny

    Mjomba wamabodza uyu.......😂😂....
    Useless mjomba

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 3 dny

    Ufela zaye boy zitaye zimenezo

  • @user-wk5oz6rr1u
    @user-wk5oz6rr1u Před dnem

    Shame on you why don't let her kut usanyamuke maka pilot loss off umunthu sinagwirizana nawe

  • @richmondchayekha
    @richmondchayekha Před 3 dny

    Inu, ma bodza bwanji, kulani , basi you think ameneyo amagwiradi ku airport, kkk, koma this is so funny, let's respect the spirit of Dr chilima to rest in peace, please.

  • @JaneLikome
    @JaneLikome Před 3 dny

    Inu ndiye simusowesedwa?mesa ndanva, zoti asilikari anaulula aja aphedwa

  • @user-hw4yw7ex4j
    @user-hw4yw7ex4j Před 3 dny +1

    Investigate nde chani ? 😂😂😂😂😂😂😂

  • @BennieMdezA
    @BennieMdezA Před 2 dny

    Mapwara ako wabodza bwanji sunanene asananyamuke

  • @AufiThera
    @AufiThera Před 3 dny

    Bas Munthu wafa kale muziti ndiululabe zatikwana sopano osangonena bwanj

  • @user-mq3mh5md5e
    @user-mq3mh5md5e Před 2 dny

    Kape iwe kape opusa bwanji siuunanene ndege isananyamuke?

  • @LYDIAPHIRIKUMALA
    @LYDIAPHIRIKUMALA Před 3 dny

    Mwachedwatu kulapako mukanalapa izi zisanachitike

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z Před 3 dny

    Ulibenso chikondi bwanji sunamutsine khutu chilima kuti asapite zongoprkazo anzako akumadziulura dzina sakuopaso ai zaziii mukuluura lero ponwe chilima wafa kale zaugalu basi

  • @hopembendela
    @hopembendela Před 3 dny

    iweyo udali ndi mwayi odziwa kuti pakufuna kuchitika chinachake unachitapo chani? dzachamba eti

  • @Mustapher-fb4qp
    @Mustapher-fb4qp Před 4 dny +1

    Usachite mantha Nena chirugamo

  • @JesusChirwa
    @JesusChirwa Před 2 dny

    Komaso or ulule pano phindu lako ndichan,

  • @FrankChindimba
    @FrankChindimba Před 4 dny

    Umboni upeleke iwe otani iwe mesa wati umaziwa zot pachitika chinachake nde ukabwere lero kumati ukudikila investigation ya mdf chilipo ufuna

  • @IvyLuka
    @IvyLuka Před 4 dny

    Zopusatu izi ngati munauzidwa inuyo ngati ndiabwino cholephela kwauza anthu okokwelawo ndichiyani

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před 2 dny

    Mbuzi izi bwanji mukuziika mu ma post ngat awa pls!!!! Ife tikufuna kunva kt chilima adafa bwanji not amphaka osowa zochitawa

  • @bandahlastone6637
    @bandahlastone6637 Před 3 dny

    God will do something punishment very soon will come

  • @AnockYunusu
    @AnockYunusu Před 4 dny

    Chakwera kille his vice president tonse tikuziwa

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q Před 2 dny

    ❤💪💪

  • @kingstonchadza6322
    @kingstonchadza6322 Před 3 dny

    Midyomba mwati mukudikira chani? Investgate😂😂 ya asilikali.

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Před 4 hodinami

      Kkkkk midyombaa😂😂😂 anyamata khalani serious

  • @EsnarthSulumba
    @EsnarthSulumba Před 4 dny

    It want change anything

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d Před 4 dny

    A shit wekha wanena kuti ndiwe msirikali chilichonse inali utawuzidwa wekhanso ukunena kuti mzanga anali atandiuza kuti china chake chokhuza ndege chichitika time zoti

  • @custommantchombe-rn1oo

    Km anthu muyalusidwa chaka chino ndthuu

  • @catherinesilverio-d5w

    Nde or mutiuze mutibwezeresa chilima????

  • @user-nr3cd7dv5e
    @user-nr3cd7dv5e Před 3 dny

    Zopepela zimenezo

  • @francis12fombe54
    @francis12fombe54 Před 4 dny

    Mukulakwa ndi mabodza anuwo Mukulakwa kwambiri muwopeni mulungu

  • @uladilimamu8351
    @uladilimamu8351 Před 4 dny

    Nde mwati mukudikira investigate? Osati investigation iyayi? Koma mmagwiradi ku airport ko?

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 Před 4 dny +1

    Uthenga wanu uli useless since anthuwo anamwalila

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em Před 4 dny +1

    Sibodza akufuna chilungamo chiyende ngati madzi, Rip Skc only God knows about ur death

  • @AnnieEssa
    @AnnieEssa Před 3 dny

    Iweyo wakupha bc😂😂😂 komaso zomabwera ma social media kumanamiz anthu mupole naso moto iwe ndiwe galu

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq Před 4 dny

    Iwe mboliyako wava kodi dzikachitika mabodza basi bwanji sumaudza kutindegeyo iwapha

  • @user-nr3cd7dv5e
    @user-nr3cd7dv5e Před 3 dny

    Iwe sumauza anthu bwa

  • @ShelaMsachi
    @ShelaMsachi Před 4 dny

    Amalawi tiyen tikule pang'ono.

  • @MosesFrancisco-q6i
    @MosesFrancisco-q6i Před dnem

    Kungofuna kutchuka etiiii

  • @HanafieMustafa-s7h
    @HanafieMustafa-s7h Před 4 dny

    Udali kut kale lonse lija sumayankhula wachamba iweti

  • @HaliJana
    @HaliJana Před 4 dny

    AKAMAOELEKA U MBONI BOX INALI MU NDEGE IKHALEPO NDIPO MUPEZEKE MA VOICE LICODAR ONSE NDIPOMWE TINGAKHULUPILILE KUTI NDI ZOONA ZOMWE AKUNE, KOMA NGATI BOX PALIBE ASALANKHULEPO KANTHU PLEASE TIKUPEPHA KUBOMAKO

  • @AlinafeChibwana
    @AlinafeChibwana Před 4 dny

    Ndiye ndindani adakuuzani zimenezo kut siibweleranso

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x Před 4 dny

    Waboza uyu video akuinenayo si kamuzu airport ndipo bdi video yakale kwambili

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 Před 3 dny

    Hahahahaha poor imformation apa zikuonetselatu kuti mungopeka nkhani palibe mukudziwapo l think mukutumidwa cholinga kufuna kuipisa mbiri ya anthu ena

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Před 3 dny

    Boza iwe

  • @user-eo8bz9xu2q
    @user-eo8bz9xu2q Před 3 dny

    Zaziiiiiii palibe tsogoro

  • @lonjezomainjeni5803

    Mbuzi yamunthu

  • @user-hs4bm2yj8r
    @user-hs4bm2yj8r Před 4 dny

    Mwafasatu ndi bodza lopanda nalo manyazi

  • @ClementbWatches
    @ClementbWatches Před 4 dny +1

    Iweso udampha nawo. Iweyo umaziwa zisanachitike nde umalekelanji kuwauza anthuwo kut asakwele ndege. Aaaàa kumaziwa kut anthu akupita komphedwa zooona osaulula.

  • @MasterHeadson-ki7ji
    @MasterHeadson-ki7ji Před 4 dny

    📌

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 4 dny

    Chilungamo chizibwera basi

  • @BatumeoMsampha
    @BatumeoMsampha Před 4 dny

    Opusa iwe

  • @Short1212-ny4ng
    @Short1212-ny4ng Před 4 dny

    Kunama iweokupha tikusaka unenebwino zonamazo ayi

  • @MoffatSolomon-p3x
    @MoffatSolomon-p3x Před 4 dny

    Koma ya ziveka tiyenazoni nyasi saphimba

  • @user-hk3hg1to4e
    @user-hk3hg1to4e Před 4 dny

    Zaziii

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 4 dny

    NGATI NDIZOONA UKUNENAZI IWENSO NDIWE MUNTHU OIPA BWANJI OSAWAUZA ANTHUO NDEGE ISANANYAMUKE ,KUTI APULUMUKE ,? NDIYE UKUBWERA LERO ANTHU TALUZAKALE MIYOYO ,. UTIUZA CHABWINO KOMA UNALAKWITSA

    • @AliceMbewe-yi1pw
      @AliceMbewe-yi1pw Před 4 dny

      Sindikumukhulupiliradi uyu tongue imeneyi si azanthu Ali jonz wa komaso nthawi yomweyi anatani kudziwitsa ilakweilakwe 😢

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Před 4 dny

      @@AliceMbewe-yi1pw ndipo inu wadya chamba uyu anthu azitenga ngati choseweresa

    • @AliceMbewe-yi1pw
      @AliceMbewe-yi1pw Před 4 dny

      @@HalisonSolomon azionesa nkhope osamangoyankhula onena chilungamo sadzaopa kose tiyeni tizingogwira maganyu ana tizasiire chuma osati mabodza aaa osamuombola munthu kumamuona akupita ngat amadziwa bwanji

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Před 4 dny +1

      @@AliceMbewe-yi1pw kkkkk ndio ndi zoona ngati akhuta azikangolima

  • @MarthaBanda-ye4pt
    @MarthaBanda-ye4pt Před 3 dny +1

    Vuto la ife Amalawi ndi limeneli timadikira choipa chichitike then tiziyakhura zambirimbiri pamene mudaona zithuzo munakanika bwanji kuuzako munthu or modzi kuti mupulumutse miyoyo yosalakwayi pilizi ...........Chilima maliro Ake ovuta kuiwalira lero kubwera izi mawa kubwera izi eeeeee😭😭😭😭😭🙌

  • @EmmaWilima
    @EmmaWilima Před 3 dny

    Opusa iwe unene pano

  • @KumbukaniMantchichi-dw2ef

    Man zimenezo mukanaulula before ndege kunyamuka apapa mungotiwawisabe mitima

  • @RomeoPrecious
    @RomeoPrecious Před 3 dny

    Msana wamak

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před 4 dny +1

    Ndelelo ngakhale ulule chilima sazuka ukanapulumusa ndiweo koma ulinditima oipa iwe

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před 4 dny

    Zaziiiiiiiii

  • @happychimwemwe-1805
    @happychimwemwe-1805 Před 4 dny +2

    Koma bwanji simunadziwitse

  • @planbkhamisolo2734
    @planbkhamisolo2734 Před dnem

    Chabodza ichi and we can't believe what you're vomiting here today
    why today ?
    Why not the very same day you were told those nonsense?
    Why not exposed the fucking plans to save those people's life?
    Ndinu zitsilu nooonse amene mukuchuluka nzeru pano pamene taluza kale miyoyo yaanthu ofunikira yet you were there keeping secrets.
    To hell with your evidences!!!

  • @user-ir8dd8lm1c
    @user-ir8dd8lm1c Před 4 dny +1

    Mutha kunyozla zili zooona oky

  • @user-rq9vc5yu7f
    @user-rq9vc5yu7f Před 3 dny

    Boli yako

  • @masakaunga4099
    @masakaunga4099 Před 4 dny

    Bodza basi

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 4 dny

    Wabodza uyu

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @bandahlastone6637
    @bandahlastone6637 Před 3 dny

    God will do something punishment very soon will come

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

  • @PriscillaKamonga
    @PriscillaKamonga Před 4 dny

    Munthu ukuchita kulephera kulankhula English 😅

    • @HEZEKIADZIDZI
      @HEZEKIADZIDZI Před 3 dny

      Inuyo ndi achitsiru kwambir inuso mukuyenela mufufuzidwe ogwila ntchito ku airport osapita ku school koma anthu inu mwakhala bwanji English kudzaza mkamwa kkkkkk anyway koma zomwe ukukambaso zizakupweteketsa kumayankhula zinthu za nzeru osat zopepela choncho ayi