Ndize Pafupi Pa (Lyrics)- Emmau Church Choir RCZ Kamwala-Lusaka

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 28. 03. 2023
  • @chrisbau4411
    Ndize pafupi pa Mlungu wanga is another favourite traditional hymn in the Reformed Church in Zambia and CCAP in Malawi. A self conviction to draw closer to God in whose care we find refuge. An English version is Nearer my God to Thee. Be Blessed and to God be the Glory.
    HYMN No. 33 (RCZ / Nyimbo za Mulungu -Malawi)
    1. Ndize pafupi pa Mlungu wanga
    Ngakhale pa mtanda mundikweza,
    Koma ndiimbabe, Mbuye mndikhalitse
    M'fupi ndinu.
    2. Ngakhale kuthengo ndasokera,
    M'dima ndigonapa, E! pamwala:
    Koma m'kulotako Ndyandikizanso
    M'fupi ndinu.
    3. Pajapo ndipenya, pokwerapo
    Angelo atsika kumwambako:
    Ndiwo akodola, Kuti ndikabwere
    Kuti ndikabwere M'fupi ndinu.
    4. Tsono poukanso, Wokondwatu,
    Ndipeza pomwepo, Pali Mlungu:
    Ndipo masautso andisendezanso
    M'fupi ndinu.
    5. Pena pakufadi, N'kwera mwamba,
    Dzuwa ndinyenyezi zitsalira:
    Pomwe ndiimbanso, Ndiza pafupipa,
    Ndiza pafupi pa
    Mlungu wanga.
  • Hudba

Komentáře • 62