Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
Mayi Patricia kariati, please musalore kutenga unduna timakukondana kwambiri and we don't want to loose you mum,
Mai Patricia dyera inu apita amenewo amakonda dyera asalaso iweo akuona ngat asakhira dala km zawo mwinanso ndizomwezo
Uthe mgwilizano nthawi yabwino before next year
Chikangawa Congress party mgwirizano uthe basi Mphaka sayenda ndi Khoswe
Gwirizano uthepo fisi ndi gwape sayendera limodzi😂😂😂
Ndi khumbo langa Kuti a UTM musalolere zimenezo please chonde
inu mukangorora ma udindo amenewo ndinu amfiti komaso simukonda dziko lanu.apapa palibe kunyengererana ayi.Mgwilidzano uthe
Yeah mrs patricia you be follow mind of mr chilima
Mai kaliat agwa mmayeselo apa koma to my opinion izi asalore ayi .....
Mayi Kaliati Chonde stand firm behind UTM. unshaken
Chikangawa party kkkkk mwadzuka bwanji
Uthe!!!!!!! Ndatii iyaaaa chipani chakuphaaaaaaaaa
Volume 😂😂😂😂
Nkhani ya bwino timve kuti zitha bwanji
Mcp ndale zawo akuti amapanga usiku
Mwayamba kunamatu a Ntanyiwa. Ma TV onse asonyeza an Anti-corruption ali ku Immigration.
Koma nde uthetsedwedi Mai kaliyat musalore chonde mzimu wa Chilima ukukwiyirani
Good decision
Good idea on this plan.
Which plan dear
Omukonda Saulos Klaus Chilima awoneka but I trust madame Kaliayi she can't accept those trapped positions with her team
Good move
Kuthetsa mgwirizano ndi MCP ndi advantage ya DPP
Kkk bolabe kusiyana ndi Chikangawa
Atambala nanu muona za chilima kumukhulukila milandu mapeto Ake anamupha naweso uziona
Kkkkk yomweyo garu iweeee
Hhhhhhhh yemweyo galu iwe kkkkkkk move ya boooo😅
Chonde a utm musalore asiyeni a MCP akhale nao mai nduna ao kwatsala nthawi yochepa musangalala pompano
Yomweeyo galu iwee!
Km mayi kaliyati Akane zimenezo aaaa anthu oyipa amenewo zopusa zimenezo
Uthepo mgwirizano umenewu
Ulemu wanu bigy
Uthebi basi
Achita bwino kwambiri kuthetsa
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Gwilizano wa UTM ndi Tonse watha lero
Musalore akweni maudindo amenewo paja anakuchotsani mwachipongwe agaru amenewo
Thesani
Achita bwino
Chonde chonde mayi kaliyati musalore unduna tikadari kukondani mama
Apa mcp ilimumadzi mukhaula
Osalora mukalora mwaitanira mtchetche pabara mumezedwano amoyo mutengere chisadzo Kwa chilima osangona chonde a UTM mukavomera mukavomera tiziwa kut chilima simumakonda mumakonda mwachinyengo don't do that please
.
Mai kaliati sangakane unduna ndiwadyela walowa kale uyu MCP
mkunamizana mawa ndilero tiwona ngati athesadi mlomwe boza mmmm
Shame on you
Mcp ma devils okha okha