BON KALINDO LERO PA 12 AUGUST 2024 |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 104

  • @AlexGomani-ss5nj
    @AlexGomani-ss5nj Před 29 dny +3

    The DC!! keep on doing a good job my president

  • @user-cg5ml7ym4v
    @user-cg5ml7ym4v Před 28 dny

    Tili pambuyo panu DC ❤❤ dziko lopempha silikhala anthu

  • @Yamikie-yamikie
    @Yamikie-yamikie Před 29 dny

    Aaaaa kma kalindo, nde zugwirizana bwanj kluza ku chipan nkupanga convention

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Před 29 dny

    Mr president nkalindo and mtanyiwwa together with mtambo Mr nkaluwaw utenga wanga ndiwoti ashankwela angompedwa nawosso shifunkwa ashimwendo banda ndallama simene ankungwilisa nshito ndisa ashankwela nosse amenne muli pha line yyot muphedwe ashankwela ndi amenne ankutumaso nkungot andu 4 ankasowa ndishankwela nayeso asowew sirriuass tonse ndi amalawi nkumanga andu nkoterenku kd ndi nkudya Sima nkwa dayllry km saywalla nkt ndege ikankalla maleley ngakalle ntunda wuntallinke bwanji km intella phasi eny time uthenga walullelle nkwa comet yya mcp live now from estan cap sauth Africa mtanyiwwa osawopha bakili muluzi TV osawopha nkalindo osawopha SINKOLI ndi llanuw nonka mbussi yophanda nselu ngat ashankwela

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 Před 29 dny +2

    We want leaders like Bon not ordained to the edicts of timidity

  • @GerladMakayika-on5rt
    @GerladMakayika-on5rt Před 29 dny

    Big up DC

  • @IbrahimSaid-h4c
    @IbrahimSaid-h4c Před 29 dny

    Umakwana President wanthu

  • @JonesMatthews-p6p
    @JonesMatthews-p6p Před 29 dny

    Opposition that's our Malawian problem

  • @HalimaMtewa
    @HalimaMtewa Před 29 dny

    Timakunyadiran abon kalindo muzipitilizabe kutiyimilira, mwana wo oooooopya.

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Před 29 dny

    The DC muzimuvela ❤

  • @solobertkamunga2826
    @solobertkamunga2826 Před 29 dny

    Dziko lake lit amapanga resign akaluza udindo wachipani, bwana DC Mwaonjeza drama

  • @macrolliekalipinde6752

    Go deeper Mr DC

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Před 29 dny +1

    Is our president kalindo thanks for your support Malawias

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 29 dny

    Kaliati Amukonzela Chiwembu a MCP Aziyenda Mosamala kwambili

  • @MecyMalothi
    @MecyMalothi Před 29 dny

    The DC akukuputa chita nawo

  • @NoorRasheed-re5vh
    @NoorRasheed-re5vh Před 29 dny

    Nkhanizi Zimakhala zongopeka kufuna kuwasokoneza anthu opepela alibe nzelu

  • @AmosMkandawire-re9pw
    @AmosMkandawire-re9pw Před 29 dny +1

    The DC tell them the truth

    • @Lingstone-r3z
      @Lingstone-r3z Před 29 dny

      Number one,,,,,, well done ✅ excellent news very much to stand on BRIGHT side

  • @AbdulrahimoMassamba
    @AbdulrahimoMassamba Před 29 dny +1

    Chenjezo lonveka ilo!!!,ma opposition sindiziwa mukumanva bwanji ino si nthawi yoyang'ana udani wanu koma kuchitira chifundo amalawi osauka. Plz 🙏 🙏 🙏 😊

  • @InnocentKadoma
    @InnocentKadoma Před 29 dny +3

    😂😂😂😂Auze live the DC mwana oooooopsaaaaa kwambiliiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Před 29 dny

    ❤❤ the deceeee

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 29 dny

    Akutitu inu a MCP mukalimbana ndi the Dddddd Cccccc!!!! Muona chinameta nkhanga mpala and musazanene kuti the DC sanakuuzeni

  • @ERICBISHOPJERE
    @ERICBISHOPJERE Před 29 dny +4

    That's true brother on electricity issues. We have been waiting for so long nothing is coming up. Watching from mzimba, Engalaweni boy.

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Před 29 dny

    Mr president nkalindo ulemu wanuw phamodsi ndi Malawi festival osawopha osavowonka ndive amalawi mulungu adalise inuyyo nosse nkumene mulinko my Allah bless you always

  • @user-us8um2gr5d
    @user-us8um2gr5d Před 28 dny

    Akunena zowona asalore kuyesa zisankho. Zisankho sizimayesedwa oppostion please take this message serious. zomwe akunena Bon Kalindo ndizowona

  • @GiftRashid
    @GiftRashid Před 29 dny

    Umakwana bon

  • @MercialWyson
    @MercialWyson Před 29 dny

    Ndiye wati ukazafa azakumbe pachulu

  • @YusufMapata
    @YusufMapata Před 29 dny

    zawo zimenezo anatuma ndani kuti akatenge ngongole ya katapila

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 29 dny

    Iwe uyambise chipani chako tizakuvotera ife

  • @HildaMachinjiri
    @HildaMachinjiri Před 29 dny

    ❤❤❤🔥

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Před 29 dny

    Koma Emusipi iyaluka Chaka Chino

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 Před 29 dny

    Kkkkkk nde mwat anatumiza njuchi ndindani????

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Před 29 dny

    Komano guys mungandionetse tsogolo la ndale za 2025 kuti zidza khala zotani
    Mwina maso anga akuona molakwika ndikaonetsetsa chipani chilichonse muli nanzikambe

  • @Mercy-mp9qy
    @Mercy-mp9qy Před 29 dny +1

    🔥🔥🔥 Much respect the DC....ofunika njuchi zitulukeeeeee😂

  • @StiviNandewe
    @StiviNandewe Před 29 dny

    Zilibwino apo a DC

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 29 dny

    Kkkķkk The DC Bon kalindo number one ❤

  • @user-sr4fe5bb2w
    @user-sr4fe5bb2w Před 29 dny

    Chitsiru ichi

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c

    The DC

  • @solomonkandiero6357
    @solomonkandiero6357 Před 29 dny

    Tell them reality😎

  • @SparrowBanda
    @SparrowBanda Před 29 dny

    Komatu za machine akunena DC zo please musalore anyamata a opposition muzalira

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 29 dny

    😂😂😂😂😂😂😂 arangize aziwebasi 17 😂 2:17

  • @EmmanuelMalata-r4j
    @EmmanuelMalata-r4j Před 29 dny

    President wathuwathu nyoooo auzeni bwana kuti anvesese kakakaka ❤❤❤❤

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Před 29 dny

    Tiona zinthu ulendo uno ndithudit.
    Bon Kalindo 🔥❤️

  • @MussahAkimu
    @MussahAkimu Před 29 dny

    More fayaaaaaa Mr nyoooooooooooo umakwanaa ❤❤❤❤❤

  • @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un

    LIve kalindo ifeo ndi ana opserapo hvy mulanje sigawa masiwiti azayese matuvi awowo azaona zokuda

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi Před 29 dny

    Mcp ndi chipani cha mtopola kwambiri iwowo conversion yao wakasokoneza ndan? Ndichifukwa tikuti mcp ndiyolephela bs

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Před 29 dny

    DCCCC!!!! THE NYOOOOOO!!!!
    INU A MCP MWAPANGA CONVENTION YANU POPANDA OKUSOKONEZANI CHIFUKWA CHANI MUKUFUNA KUSOKONEZA CONVENTION YA DPP??? MULIBW MANYAZI TIZINGOMVA ZA INU MU DZIKO MUNO?? ZITSIRU INU ASYENI A DPP AMASUKE MU DZIKO MWAWO. AGALUUUU INU.

  • @user-rd2td7bg4c
    @user-rd2td7bg4c Před 29 dny

    The DC timakunyanila ❤❤ from mulanje.limbuli

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 29 dny

    Komatu Inu a mcp phuzilani kukhala athu atetendele chonde Inu mwapanga yanu covetion yanu palibe yemwe wakusokonezani Inu chifukwa chani muli athu oipa Inu mmm ayi mudziweni yesu ndi ophuzila Ake 12

  • @user-js6xn9qj1r
    @user-js6xn9qj1r Před 29 dny

    The DC mwana oopsa kwambiri President of the poor people, BK tulutsa njuchi chonde zilume makapewaa

  • @LeonardTambala-n9d
    @LeonardTambala-n9d Před 29 dny

    Mbambande kungalula 😅😅😅😅

  • @user-pz4py6ew6z
    @user-pz4py6ew6z Před 29 dny

    Yomweyo Mr Kalindo mumatiyimilila ife amalawi❤

  • @DeviLinya
    @DeviLinya Před 29 dny +1

    Kkkkkkkkkkkkkk uli bho ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Před 29 dny

    Umakwana mwana wakwathu iwe ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @DubeSitolo
    @DubeSitolo Před 29 dny

    Ndie mwat inu siosewela nanu

  • @PaulKalambo
    @PaulKalambo Před 29 dny

    The DC mutayimila mpando wa u president mdziko muno I hope mukhoza kupambana

  • @BesterDaude
    @BesterDaude Před 29 dny

    Mfumu

  • @XimbaXimbaa
    @XimbaXimbaa Před 29 dny

    Layton mangochi angakhale akulubwa lubwa sangayambepo pa bon kalindo dc

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw

    The DC iiiiiiiiiiiiii on fire auzeni Agwawao kkkkkkk apange resign

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před 29 dny

    ❤❤❤❤❤❤love Dc😂😂

  • @Maliet-nh6kf
    @Maliet-nh6kf Před 29 dny

    😅😅😂😂😂zikhale h

  • @EusébioLucianoGaiondo

    Born kalindo 🔥

  • @StrongboyDaud-wr1sh
    @StrongboyDaud-wr1sh Před 29 dny

    Utenga wabwino kwambiri from the DC

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw Před 29 dny

    The Dc big fighter chilungamo

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Před 29 dny

    Ndipo palibe kuyeselera machine, maganizo amenewo palibe yemwe angalore zayamba liti zoyeselera machine za uchisiru.

  • @samhussen708
    @samhussen708 Před 29 dny

    😂😂😂 the DC kkkkkk

  • @IssahDavie-o8q
    @IssahDavie-o8q Před 29 dny

    Aphwetekeni bs osanyengelela the DC

  • @KondwaniMamveka
    @KondwaniMamveka Před 29 dny

    Kkkkkk🤣🤣🤣🤣🤣

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 29 dny

    Iwe ndi one Hiyaaaaaa de DC nyooooooooooo went weni mwana oipitsitsa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AmosMkandawire-re9pw
    @AmosMkandawire-re9pw Před 29 dny

    Zoooonaaaaaa Dc

  • @violetpotani
    @violetpotani Před 29 dny

    Awatu akusewera oho akagwera ku chiphompho

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před 29 dny

    ❤❤❤kuwuzatu onse❤❤

  • @MohammedAriesa-h8s
    @MohammedAriesa-h8s Před 29 dny

    More ❤❤❤❤

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 29 dny

    Njuchi zomwedzo kkkkkkkkk aziona chaka chino 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 29 dny

    Akufuna kukasokoneza convention ya DPP wo asakabwerere amoyo

  • @BesterWilliam
    @BesterWilliam Před 29 dny +2

    This is dpp man

  • @ClementHaneef
    @ClementHaneef Před 29 dny

    Mwala zipita koko xikalume

  • @AbdulMustafa-k4f
    @AbdulMustafa-k4f Před 29 dny

    Katundu iweyo timaziwa za bon kalindo

  • @SammieDickson-ln2hp
    @SammieDickson-ln2hp Před 29 dny

    Km DC amakwanira ndipo akulikonda dziko lathu

  • @YamikanBanda-z7z
    @YamikanBanda-z7z Před 29 dny

    Mbambande bon

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 29 dny

    Waboza iwe mulungu akuyendele

  • @MemoryLikaka-to7ho
    @MemoryLikaka-to7ho Před 29 dny

    😂😂😂

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Před 29 dny

    MCP ikadali ndi ma plan osaka anthu mmmm

  • @AlieSaidmussa
    @AlieSaidmussa Před 29 dny

    Tawauzeni

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani Před 29 dny

    Katundu

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Před 29 dny

    Akatundu the dc

  • @MphatsowisikiWisiki
    @MphatsowisikiWisiki Před 29 dny

    Mbambande mmesa

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune Před 29 dny

    Otumidwa

  • @LacxyAscott
    @LacxyAscott Před 29 dny

    Kkkkkkkkkkkk

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 29 dny

    Komaso nkhani zomwe amayakhula akulu awa siziveka tathauzo yake

  • @DalitsoMichongwe
    @DalitsoMichongwe Před 29 dny

    The Dccccc ccc cccc😂😂😂

  • @HassanYusufu-q4f
    @HassanYusufu-q4f Před 29 dny

    Timakunyadiran bwana

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Před 29 dny

    The DC

  • @LeonardTambala-n9d
    @LeonardTambala-n9d Před 29 dny

    Mbambande kungalula 😅😅😅😅

  • @CatimboJosé
    @CatimboJosé Před 29 dny

    The DC