NSOKHANO WA UTM LERO12 July 2024 ANTHU ALUSA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 07. 2024

Komentáře • 57

  • @MadalitsoAction
    @MadalitsoAction Před 23 dny +5

    Good kwa good timaona ngati simudamudzindikire usi kuti ndi wa mcp congratulations UTM

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Před 23 dny +5

    Zilibwino kwambiri muwasiyedi achina chikangawa adziyezekana okho okha ❤❤

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d Před 23 dny +2

    Mulungu adati usaphe, wakupha sapeza mtendere. More fire ❤

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Před 23 dny +2

    If you have been following MCP, since they took powere ,the day that MR CHAKWERA elected as the president of MALAWI , it's the alliance was ended. It was only people of UTM and there heart of love ,that is why they were behind following MCP . But MCP was not countef UTM as there helpers who gave power to bring MCP .in the Government .
    My advice to UTM PARTY MEMBERS ,make sure when you go to DPP,AFORD,UDF ,share the sits before you enter in the Government . Doesnt matter we never know what the out come results will be . But do everything in advance to avoid what has happend eith MCP. We know this sits of PRESIDENT IS VERY SWEET LIKE YOU ALREADY IN HEAVEN WITH JOHN AND HIS FRIENDS.

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Před 23 dny +1

    Thanks for good dission ❤❤❤❤ live satanic chakwera & onther look forward....don't scred

  • @user-hu4gu7op7n
    @user-hu4gu7op7n Před 23 dny

    Woow thus vry good idea, lets push together is one👍

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em Před 23 dny

    Viva SKC viva in heaven, UTM is not canna die, rest in peace our freedom fighter

  • @user-vr9mj1tu1u
    @user-vr9mj1tu1u Před 23 dny +2

    Zilibwino kwambr ndizimene timafuna🎉🎉

  • @HalilullahRichman
    @HalilullahRichman Před 23 dny +1

    Ineyo sindisata kwambiri za ndale but this dicition is quite alright
    Zandisangalasa

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 23 dny +1

    Very good UTM Chakwela you mast go watikwana ❤

    • @adammadi8248
      @adammadi8248 Před 23 dny

      Zilkomo akweni ndili nanu ndithu.ine ndebvu ndiizochuluka ndithu.

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 23 dny

    Osabwelera mmbuyo❤❤❤❤ moto kuti buuuuu UTM yomweyo

  • @user-zg6mn8qr4m
    @user-zg6mn8qr4m Před 23 dny +1

    Congratulations UTM

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Před 23 dny +2

    Chakwela akapange ndi agogo ake alliance

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s Před 23 dny +2

    Very good very good very good

  • @user-hl1jt6eo3d
    @user-hl1jt6eo3d Před 23 dny +2

    Zilibwino kuthetsa tonse alliance. MCP anthu oipa

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i Před 21 dnem

    Very good from kuno ku mpoto

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 23 dny +2

    Yaaaa zikufunika kuti amalawi azikhala olimba mtima chonchi zilibho basi

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Před 23 dny +1

    Achilima zozani anthu akhale olimba tima ngati inu zimuwanu uwakute onse

  • @GMw-t5h
    @GMw-t5h Před 23 dny +1

    Kuipatsa moto ku 💥💥 koma kwatelera 2

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 23 dny +2

    Mwachita bwino kwabasi kutuluka chifukwa munakatheramo

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 Před 23 dny +1

    Congratulation UTM

  • @ChawezChinkhuntha
    @ChawezChinkhuntha Před 23 dny +1

    We trust eMama kaliat

  • @user-ug6ox9rf7c
    @user-ug6ox9rf7c Před 23 dny +1

    100 /100

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před 23 dny +1

    Gay's musalimbane ndi kunyoza UTM chifukwa ndikufuna ndikuzeni moopa mulungu Kanda UTM chakwera sakanawina ine sindikonda za ndeke koma chilungamo chiyende ngati madZi

  • @charleslimbani8590
    @charleslimbani8590 Před 23 dny +1

    Chuma cha masiye sichichedwa kuthaaa.....Chilima palibe amene angatengeee mzeru zakeee ....inuyoo zanu zikharaa zanuu ....musanamizee a Malawi kuti axakupaseni mipandoo kenako muzawaputsitsee.......

  • @mathewsmakina7845
    @mathewsmakina7845 Před 23 dny +1

    Ndizimene timadikila

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Před 23 dny +1

    Zabwino zilitsogolo mulungu wamakamu alinafe alekeni ankhale nacho chipanicho ndipo zilibwino aziona amenewo

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 23 dny +1

    Boma lilibe ndalama zowonga just for to find out nothing gonna rise up chilima

  • @LawrenceMvula-xj5ex
    @LawrenceMvula-xj5ex Před 23 dny +1

    Go deeper 🎉

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 Před 23 dny +1

    Tasangalala ndi UTM potuluka mu mgwilizano

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 23 dny +1

    Zayenda bwino agaluwa atikwana achoke basi.......chakwera simunthu wabwino ayi ....ayi mmbusa zausiru basi

  • @YamieTiyesi
    @YamieTiyesi Před 23 dny +2

    Tembenuzani galeta ndalasidwa

    • @user-im7sc2my4w
      @user-im7sc2my4w Před 23 dny

      😂😂😂,yinakuwa mfumu ,APA ndiye tinalasidwadi yooo

  • @jonathanmasangano4559
    @jonathanmasangano4559 Před 23 dny +1

    Zili bwino kwambiri

  • @lacqueymalley2674
    @lacqueymalley2674 Před 23 dny +1

    Amen

  • @user-vw7tj2ss3l
    @user-vw7tj2ss3l Před 23 dny +1

    Zaka 30 Ali kunja anaiwala

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica Před 23 dny +1

    Ananena kuti kuti usi sapite?

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 23 dny +2

    Amalawi sleeping, utm panokha never gonna take Malawi forward

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 Před 23 dny

      Tilibe name ntchito we will stand as UTM forever!

  • @HhhMas
    @HhhMas Před 21 dnem

    Zonse boooooo

  • @TemboHaswell
    @TemboHaswell Před 23 dny +1

    Zimene timayembekeza ndizimenezo🥴🥴🥴

  • @HassanMbalaka-gb5sv
    @HassanMbalaka-gb5sv Před 23 dny

    Were is manganya

  • @BlackSpiderujayo
    @BlackSpiderujayo Před 23 dny

    Michael Usi Yudasi skaliyoti

  • @AustinKaponda
    @AustinKaponda Před 22 dny

    Zoona nafeso tatulukamo mmenemo ndikuzenje kumeneko

  • @davidkasisi7490
    @davidkasisi7490 Před 23 dny

    Ndimakonda UTM ndizakhala ndikuikonda mpaka kale

  • @anicakandiado
    @anicakandiado Před 23 dny +2

    Wozawoza🥳🥳🥳🥳

  • @lloydkamwambi1804
    @lloydkamwambi1804 Před 22 dny

    Micheal usi ndi wa mcp ndipo mumuuze panya pake ndipo sitimuopa ayi

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Před 23 dny +1

    Munda wa chitedze sasosa ayi amangowontcha basi

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 23 dny +1

    Chipan kuvera anyamata amasamba achezo kkkkkk mwamaliza chipan anthu Inu ndithi

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 23 dny +1

    Akaliyate kumaliza kochuka mboma mdikomweko palimbepo chipan chingatuluse mcp boma zosatheka muenera u vs president omwewo osat kudziyimira panokha ay

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 23 dny +1

    Maganizo opusa utm, basi utm yatha just know that

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Před 22 dny

      Kagwere yatha kunyumba kwa amako mwana Wa njoka iwe

  • @jonathanmasangano4559
    @jonathanmasangano4559 Před 23 dny +1

    Zili bwino kwambiri