Times Exclusive with Felix Njawala - 21 January 2023

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024
  • Times Exclusive with Felix Njawala - 21 January 2023

Komentáře • 23

  • @MuyaoComedies
    @MuyaoComedies Před měsícem

    I'm following Salam alaikum

  • @Alilevati2994
    @Alilevati2994 Před rokem +2

    Koma brian banda amwene 😂😂😂🙌

  • @asheemashley598
    @asheemashley598 Před rokem +1

    Pali bvuto kwa atsogoleri athu amangofuna kt bola alowe kenako azipanga za zofunika zao.Amalowa m' boma cholinga kt alemere bas

  • @petersonmatumbo3757
    @petersonmatumbo3757 Před rokem +1

    Aaaah mbuz yamunthu

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Před rokem +3

    Hahahahaha 😂 😂 zikuvuta pati ??? Tayankha galu iwe one million jobs yilikuti

  • @mortonbaloyi9202
    @mortonbaloyi9202 Před rokem

    10 years with chilima is enough .he has failed us

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Před rokem +2

    Vuto lomwe lili ndi Amene mukut dr wanuyo kay udocter wachiyan mukut chilimayo amat akangokhumudw amayamb kulul akt wakut akub pakut pakubedw akasiyidw bas amat ziii what tip of utsogoler oteroyo
    Ine chilim ndimamukond koma panop ndinyas kwainey i dont lik him ndimunth wabodz

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Před 6 měsíci

    Chilma bomaaa

  • @paulchimenyera5553
    @paulchimenyera5553 Před rokem

    UTM member weni weni
    Sasintha ma wanga
    Same like ukalowa mupingo sumasintha ngati zovala
    Even mu banja mumatha kuyambana koma ngati kusiyana
    Musiya Akazi angati or Amuna Angati

  • @pauldaka7966
    @pauldaka7966 Před rokem +1

    Palipano ku Malawi kudakalibe munthu oti akhoza kulamulira dziko fafupifupi mmene akufunira anthu.

  • @rahimmapata545
    @rahimmapata545 Před rokem +1

    Mavuto akwawona a utm nthawi zonse amenena kuti a mcp akudya wokha

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Před rokem +1

    Ndiwabodz Ameneyu
    Waiwal kt mtsogoler wao chilim ndiamen adawanamiz kt feterez adzakhal ochip
    Komanso mapaspot Anthut sadaiwal zimenez

  • @edwintshepang5108
    @edwintshepang5108 Před rokem +2

    Pachichewa Pali mau amati zathu salowa nkhola, zithu zakuvutani Basi palibe chomwe mungauze amalawi panopa ,mwangoononga malawi

    • @khumbongwira7726
      @khumbongwira7726 Před rokem

      Munthu wa mzelu zoyenelela anga peleke support Ku UTM?

    • @MercyPhiri-nh9jy
      @MercyPhiri-nh9jy Před 6 měsíci

      Amalawitu amayiwala mwamsanga Kodi Inu nonse mukunena za mademo ndimayesa anakuonesani ndi chilima omweyo

    • @MercyPhiri-nh9jy
      @MercyPhiri-nh9jy Před 6 měsíci

      Mpaka pano mwayamba kukhala nayo mbanvu yonena za ku ma khonthi

    • @MercyPhiri-nh9jy
      @MercyPhiri-nh9jy Před 6 měsíci

      Mumadziwa Inu nthawi yoseyija mesa ndi chilima yemweyo abale nthawi Zina kumayamika ndi bwino

  • @johnkamwendo2742
    @johnkamwendo2742 Před rokem +1

    Rubbish atsogoleri akumalawi

  • @emmanuelchavula7144
    @emmanuelchavula7144 Před rokem +3

    2025 SKC BOMA