ZIDAPITA UKU- KUYANKHULA KWA PRESIDENT WA MALAWI NDI MOZAMBIQUE

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 09. 2024

Komentáře • 21

  • @GanduBondu
    @GanduBondu Před 15 dny +2

    Azimai ndamene akuononga ziko😢😢😢😢

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 15 dny +2

    Kumalawi tili ndi aprezident koma tilibe nsogoleri

  • @indiAisha-q2o
    @indiAisha-q2o Před 15 dny

    Chakwela ndichikangawa wakupa😢😢 Kodi ndalamazi zinalikuti

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Před 15 dny +1

    Shame on you
    Adzimayi akumalawi umbuli sudzantha kuvina Koma mmimba mulibe kalinkonse 😢😢

  • @PempheroAlli-v8y
    @PempheroAlli-v8y Před 15 dny +1

    Vuto ku Malawi adzimayi ambiri ku school sanapiteko chfkwa uphawi suzatha

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 15 dny +1

    Mwalephera kulamulira ziko lamalawi tulani pansi udindo zomvesa chisoni anthu ena kusowa omusangalarira umbuli chani

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i Před 15 dny

    Dziko silikuyenda bwino njala yamvuta ndiye adzimayi onunkha kum'bwetsewa kumakawombera m'manja zopusa koma umphawi sizinthudi

  • @CharlesChamveka
    @CharlesChamveka Před 15 dny

    Zitsilu za wathu & chakwela wanuyo mfundo alibe kamwendo njila anadya matako agalu

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b Před 12 dny

    Azimai ovuna ndye zitsiru kod mulibe zochta?pali mfundo zanji apa zoti muombele mmanja za u hule basi

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Před 15 dny

    Boma nilomweli basi

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 15 dny

    Malawi yili pa moto, uyu si mtsogoleri ayi akulu akulu, ndipo mistake yimene tidapanga posankha fisi uyu, mmmmm kaya.

  • @user-hk4sp5tp9g
    @user-hk4sp5tp9g Před 15 dny

    Kkkkkkkkk chikangawa fundo alibe uyu

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w Před 14 dny

    Anthu akulilongwe okha ndiamene akutenga zopusa

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Před 15 dny

    Palibe kusintha chan koma iweyo ukuyankhulawe ok ok zopusa izizi tatopa nazo wina adzawona polekera

  • @SamuelBhanda
    @SamuelBhanda Před 15 dny

    Mtundu wopanda ndevuu siwabwino

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Před 15 dny

    Adzimai adzimai!!!..

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před 15 dny

    😂😂😂😂😂😂😂😂 chakudya chuvuta ngakhare azibaleako akuchisowa kumalawi kuno ayeeee kuchikanga ayeeeeee 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @GeorgeWhite-f1p
    @GeorgeWhite-f1p Před 15 dny

    Musatirakwise

  • @KennethDzama
    @KennethDzama Před 15 dny

    Citsiru

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Před 15 dny

    Bomasitikusintha