JEG - MPWECHE || Dir. by Director Tonney

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 7. 09. 2024
  • Ase Hyke
    Hyke
    Tellem look
    Pano ndinayaka Moto fire gasoline
    Married to the game namutaya Caroline
    (Jeg ndi zida Ase) hahaha lyre violin
    Am barely around ngati Kaya pangolin ?
    You nuh mean
    Checker last seen
    Lusoli mwa ifeyo nde ndi everlasting
    Awo sankatifila ena ankati Sala panopa eh they are fast in (fasting)
    Get it it's embarrassing
    Ngati sizili bho mungomwela aspirin
    Mwangondisowa chabe mundipeza pa screen
    Ka style Ka clean
    Ngati Ka kicks Ka Grin
    Braaa
    Vuto lake ma fellas
    Mukuchulusa ma jealous
    Mukungochonga ma errors
    Cholinga chanu tithe basi
    Koma ndili ma style mpweche
    Mpweche mpweche mpweche
    Mpweche mpweche
    Ndine mwa njobvu mpeche
    Mpeche mpeche peche
    Mpweche peche
    Look pa beat (ndine genius)
    Krazy (ngati phenius)
    Skill (ya vinicius)
    Kuphusha ( So ambitious)
    Yo ndili sick heavy ndili serious
    Ndili fly ndege uli minbus
    Air force 1 iwe slippers
    Ndimangoku pewani Mukuziwa izi
    Ase wise, yaizi ndiyoti
    Sinakhalapepo ,pansipoti
    Kumangochiller ,pa sipoti
    Malo mossaka , ya passport
    Asa
    Vuto lake ma fellas
    Mukuchulusa ma jealous
    Mukungochonga ma errors
    Cholinga chanu tithe basi
    Koma ndili ma style mpweche
    Mpweche mpweche mpweche
    Mpweche mpweche
    Ndine mwa njobvu mpeche
    Mpeche mpeche peche
    Mpweche peche
    Mukuchulusa ma jealous
    Mukungochoka ma errors
    Cholinga chanu tithe basi
    Koma ndili ndi ma style
    Mpweche mpweche
    Ndine mwa njobvu
    Ndine genius
    Ngati phenius
    Ya vinicius
    So ambitious
    Basi basi basi basi basi basi basi basi
    Basi basi basi basi basi basi basi basi
    Bruh
    #jegtellem #mpweche #malawi #trending #penapake #momo #balinkede #Jeg #afrobeat

Komentáře • 76