Dalitso la nyimbo iyi pa ine ndi lalikulu and nyimbo iyi ndi moyo wanga ndimangoganidza ngati anaimbira ine eeish thankh you father mwedzi uno ndibwera ndi umboni owopsa
Achita...lero pomwe mwana wanga wayamba mayeso ake a maneb a PLC ambuye achite ndithu i need selection for my son 😢😢😢😢😢. Mulungu ochita zodabwitsa achite munyumba ino...
Have had a tough period in life this year, i almost lost my life... but this song just reminds me God can never leave me... he never sleeps nor slumbers to just see me rise up sooner than I was in every situation... I thank you Lord for your mercies which are new ever morning and for your kindness in my life.
Ondisamala he never got tired no forsake me even titanchimwira motan he still cares n protect adzilemekezeka all the time amen
amen amen
Mukumane ndichosowa changa
Mukane ndichosowa changa baba
Amen amen
Chachikulu chichitikadi pa moyo wanga nd pa banja langa
Amen
God🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌I know you with me 🥲🥲🥲
Ambuye citani nd moyo wanga citonzo cikuwawa😢
Thank you Jesus, thru this lady am healed, Amen
Indeed Lord you are going to do it again I trust you I will testify ambuye mwayamba kale ndipo mukayiyamba ntchito mmayimaliza Lord I thank you.
Lord I just want to say thank you for everything you have done upon my life and to my family and what you are about to do 🙏
I love this song❤. will definitely testify to it.
😊God bless my children
We save a miracle working God this song❤
I trust you Lord
May God bless you mama
i still love song ❤
Lord Jesus you will do it again chachikulu chichitikadi i trust you 🙏
Indeed
very powerful
Woooo nice 🎉
Amen
🙏 amen
Amen..ndpo zaperekera umboni
Chaka chino 2024 tilowa m'banja 🎉
Thank you Jesus Christ of Nazareth,God of Miracles
This song healed me,thank you ❤️
Dalitso la nyimbo iyi pa ine ndi lalikulu and nyimbo iyi ndi moyo wanga ndimangoganidza ngati anaimbira ine eeish thankh you father mwedzi uno ndibwera ndi umboni owopsa
❤indeed God will never leave no forsake us my aunty introduced me to this song 🙌🤗
Achita...lero pomwe mwana wanga wayamba mayeso ake a maneb a PLC ambuye achite ndithu i need selection for my son 😢😢😢😢😢. Mulungu ochita zodabwitsa achite munyumba ino...
Nice song
Ooh I love this have been listening to it from morning until now its 21hrs
This is anointed song, indeed something big is gonna happen to me 🙏
My favorite song
Have had a tough period in life this year, i almost lost my life... but this song just reminds me God can never leave me... he never sleeps nor slumbers to just see me rise up sooner than I was in every situation... I thank you Lord for your mercies which are new ever morning and for your kindness in my life.
Safulumila ndipo samachedwadi ,mlungu ndi wazatheka bwanji
Mukumane nane baba
I have faith in GOD chichitika chachikulu in my family in JESUS NAME
Favorite song ♥️♥️♥️
I have a testimony with this song. I got job. Be praised almighty God
Powerful Song ...Sachedwa safulumila ....Chichitika chachikulu pa moyo wanga...
This is not just an ordinary song, but a heavy message
Anointed song imakufikitsa pa mapazi a mulungu ndipo subwelerapo chabe
Amen and amen Eish ondisamaladi samagona tulo
Samachedwa safulumira Mamuna yesu ndiye chiukiso🎉🎉
Amen
Coming back to this song again 😭😭😭
Mwandiilimbikitssa
I like this song,, imasitha nyengo ukakhala muchiphinjo❤