Factory265 Media
Factory265 Media
  • 17
  • 283 788

Video

Zinatani kuti oyimba a ku malawi adzingoyimba nyimbo zokopela m'mayiko ena?
zhlédnutí 2,4KPřed 21 hodinou
In this video we caught up with a legendary broadcaster Samuel Malunga Dothi to explain what happened to Malawi's music soul, that has led to having a music industry filled with music copied from other countries.
ZAULULIKA// Dan Lu waulura zinsinsi zina zomwe zikuchitika mu music industry ya ku Malawi.
zhlédnutí 56KPřed dnem
Factory265 caught up with legendary artist Dan Lu to shed more light on what has prompted him to start thinking of quitting music.
Analakwa chani oyimba awa? (Part 1)
zhlédnutí 10KPřed 14 dny
These are 5 most underrated artists in Malawi. NOTE: Sound on the song on number 2 was muted due to copyright issues.
JB ASAMVE IZI
zhlédnutí 8KPřed 21 dnem
Legendary Dancehall artist Nyakwawa Annie Matumbi speaks out
Malawi Got Talent / Uyu Mukumudziwa? J Manning - Feel Like
zhlédnutí 479Před 21 dnem
Another hidden talent from Malawi all the way from capital City Lilongwe
Mwati Mfana uyuyu Sakutchuka Chifukwa? Simba - Money
zhlédnutí 424Před 28 dny
Simba is one of the greatest talents to ever come out of Malawi. enjoy one of his masterpieces Money
Namadingo Wasowa???
zhlédnutí 14KPřed 28 dny
If you missed the previous video talking about how much money Malawian musicians are making on CZcams you can check it on this link: czcams.com/video/eHYW0yJkY1I/video.html
WE ARE FACTORY265 MEDIA
zhlédnutí 261Před měsícem
A preview of what this channel is all about
OYIMBA A KU MALAWI AKUPEZA NDALAMA ZINGATI PA YOUTUBE? - TILI NDI TOP 10
zhlédnutí 80KPřed měsícem
NOTE: Nthawi yomwe timapanga video yi tinayiwala Saint-Realest whose Estimated Monthly Earnings are at - $170 (MK294,627.68) - $2.7K (MK4,679,380.80) Kupangira inu mukudabwa kuti Dr Namadingo sakupezeka bwanji pa list ya oyimba a ku Malawi amene akulandira ndalama zambiri kuchokera ku CZcams....List yi yapangidwa posakatula oyimba okhayo amene ali pa "CZcams Partner Program" kapena kuti oyimba ...
KODI UYUYU SAKUTCHUKA CHIFUKWA CHANI? Simba - Mariah (Official Video)
zhlédnutí 4,4KPřed měsícem
Malawi's gifted dancehall artist Simba performs Maria.
Anthu Anandithamangitsa pa stage Mayi anga akuona - Nepman
zhlédnutí 41KPřed měsícem
An exclusive interview with Malawi's husky voiced artist Nepman talking about his journey into the music industry.
NKHANI ZODABWITSA ROBOT MPAKA KUDZIPHA YEKHA KU SOUTH KOREA
zhlédnutí 337Před měsícem
This is a story about the first ever robot recorded to have committed suicide in South Korea
`DNA - Mwa Iwe (Official Audio)
zhlédnutí 1,7KPřed měsícem
One of Malawi's gifted artists DNA performs Mwa Iwe released on 12 July 2024
TINAMUFUNSA MED C KUTI APANGE FAMILY YAKE YA ANTHU OTCHUKA OKHAOKHA A KU MALAWI
zhlédnutí 704Před měsícem
We asked Malawi's rising star Med C to create his celebrity family, guess who he chose as hid dad, mum, siblings and spouse.
Lucius Banda & Patricia Shanil Dzimbiri - Adzayankha
zhlédnutí 45KPřed 2 měsíci
Lucius Banda & Patricia Shanil Dzimbiri - Adzayankha
MAU AMENE LUCIUS BANDA WASIYILA OYIMBA
zhlédnutí 13KPřed 2 měsíci
MAU AMENE LUCIUS BANDA WASIYILA OYIMBA

Komentáře

  • @user-th3xn7ly3y
    @user-th3xn7ly3y Před 8 hodinami

    Zambiri wanama

  • @AdaKalinde-c4j
    @AdaKalinde-c4j Před 19 hodinami

    Umatha onesmus❤❤

  • @akonlayson3165
    @akonlayson3165 Před dnem

    The greatest Artist in Malawi

  • @MatthewKanyenda
    @MatthewKanyenda Před 2 dny

    Khalidwe longa ili ndilimene lidapanga expand mngakhale mma Radio station mwathu momwe. They promote ma artist akunja instead of local artists. Chodabwitsa mchakuti Kuti akuwerere nyimbo ndi ndalama uwapatse ma DJ, nanga R Kelly ndi DJ Tira komaso Rick Ross amakuma naye Kuti kuwapatsa ndalama Kuti adzimuikira nyimbo program yonse kutha zakunja zokhazokha.? Maiko anzathu tu sungamve nyimbo za Ku Malawi pa radio yawo. Especially mudzapite Ku south Africa then mukumvere ma Radio station awo.

  • @ibulamatabwa1607
    @ibulamatabwa1607 Před 4 dny

    Onesimus ndi dolo kwambiri

  • @isaledambe
    @isaledambe Před 4 dny

    I hope someone has written this important history on music in Malawi.

  • @ModesterWilliam-g7z

    Wati samafuna zopusa

  • @Bilton-q6i
    @Bilton-q6i Před 4 dny

    Zoonadi big man. Thanks for the info.

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn Před 4 dny

    Kuyimba ndi ganyu yabwino

  • @MohammedAriesa-x8x
    @MohammedAriesa-x8x Před 4 dny

    Onesmus

  • @VanirenDalitso
    @VanirenDalitso Před 4 dny

    You king

  • @ChizukuluMafunga-f8s

    Boss onesmas 😅

  • @SirpromiseMatabwa
    @SirpromiseMatabwa Před 4 dny

    Dolo onesmas

  • @user-dh3gr2cg4o
    @user-dh3gr2cg4o Před 5 dny

    Inuyo mumantha kuimba

  • @nicholasmanyamba416

    Well explained brother open years for ama2000

  • @PRINCE_COOL78
    @PRINCE_COOL78 Před 6 dny

    Anthu anakutuluka dan since unaimba nyimbo yotukwana ija ukuphunzitsa chani kwaachinyata manager wakoyo anatolia bwanji kuimba zopusazo

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka Před 6 dny

    nyimbo zako azikavera. ndi APM ife ai

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka Před 6 dny

    vuto ndiwekha azikuvera APM

  • @RobzyMW-b2t
    @RobzyMW-b2t Před 6 dny

    Music industry ya kumalawi sili bho anthu nsanje komabe still kumukonda Nepman ❤❤❤ amabwela bho

  • @JulietGunde
    @JulietGunde Před 6 dny

    Nkhani yavuta ndindalama😂 koma to be honest Dan Lu kalekale muja umaimba nyimbo za dzeru hvy

  • @kondwanimbewe1317
    @kondwanimbewe1317 Před 6 dny

    Well explained

  • @nkhwaziaeros1845
    @nkhwaziaeros1845 Před 6 dny

    Very informative. Its crazy i don’t know most of the artists mentioned above😢Please Malawian lets do something about recovering the old music this man has been describing above.

  • @AsiyatuAnaki
    @AsiyatuAnaki Před 6 dny

    Rashly ndi ovula

  • @Zied-u2k
    @Zied-u2k Před 7 dny

    Pano zimene mkuyimba ana ama 2 pin ife ndi mbola kuli anatu kuno akiphulisa music

  • @MahallaMinistries-fv1hw

    This gentleman deserves respect

  • @MahallaMinistries-fv1hw

    "John bwelera," what a reminder❤

  • @KennethObvious
    @KennethObvious Před 7 dny

    It is true broh akulemekeza chibwana

  • @PrinceBlessings-bv5bs

    Ndi zoona big... Pano music mmm mwalowa zina

  • @Thabiso09
    @Thabiso09 Před 8 dny

    This history of our dry music past without infusing our own traditional dances can assist our youth into driving music onto the world map

  • @AmadumtungasudiSudimtungaamadu

    Mumatha ndpo tlip ambr okhala kumbar yanu zandaleazitengele ku music aaaa sbwn😢😢

  • @AmadumtungasudiSudimtungaamadu

    Kuzolower kupondelezana bc malawi🤪🤪🤪🤪

  • @MayimunaZuber
    @MayimunaZuber Před 8 dny

    Zabwino zonse brother musiyedi kuyimba mwapanga chisankho chabwino

  • @user-ih3qe8ho3v
    @user-ih3qe8ho3v Před 8 dny

    Dan Lu old song was very fantastic but now mmmmmh whow bad😢

  • @AaronKalambo
    @AaronKalambo Před 8 dny

    czcams.com/video/DQJz60r2i_c/video.htmlsi=LxUJOsc3vetZLjZP

  • @actuarialscience2283

    Akunena zoona ndinamva nyimbo za Aran Namoko ku Kenya koma mu language yakomko. Ndinadabwa.

  • @actuarialscience2283

    Angakhale Jetu amayimba za ku South Africa

  • @actuarialscience2283

    Bambo tchende pamtumbo/pamphumi. Ineyo ndili ndi PhD yotukwanayo. Iwe Mac-Hendie-son komanso Mac-haba.

  • @actuarialscience2283

    MCP ndi ufiti weniweni komanso osaphunzira ndipo anapha Chilima

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 9 dny

    Apa ndiye afotokoza bwino kwambiri ndipo ine ndakhulupirila

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we Před 9 dny

    Why hands keep on trembling

  • @user-nu3kk8xr4s
    @user-nu3kk8xr4s Před 9 dny

    You can see achina blaze ,sir Patrick even Nepman all the songs zimwe anayimba uona kut analibe youtube channel they just open now these years see so expect pple to subscribe and yet carrier yawo ikupita kokuntha aaa no way thy need to follow music business osamazitenga chizolowezi

  • @user-nu3kk8xr4s
    @user-nu3kk8xr4s Před 9 dny

    Most of these musicians thyr dnt know how to run there music as business so instead of going on digital to sell they music thy just being lelax with songs zikamaveka ma burning centre artist them selves thy have to blame themselves

  • @michaelnazimera7231

    Inu mumatha bro kuyimba osafooka ai

  • @ConeriasPhiri
    @ConeriasPhiri Před 9 dny

    Akufuna angopuma awa

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před 9 dny

    Poor man's soup 🍲😂😂😂 big Up brothers

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 9 dny

    ziri bho kwambili

  • @VictorWiness
    @VictorWiness Před 9 dny

    mbiri yokoma ndthu zapamwamba izi pitilizani kufukula mbiri

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 Před 9 dny

    Zilibwiino kwapili kwajema Malawi watuu ❤❤

  • @Dali-Damson98
    @Dali-Damson98 Před 9 dny

    Koma peter bandayo😊

  • @PreciousMangulama-l4i

    Mr lufani musatisiye musakwiye musa foke tihansizeni tima phuzila zambili kwainu